WORLDstudios

WORLDstudios Music production

 Mayi wazaka 38, Esther James, amugamula kukakhala ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi kaamba kopezeka olakwa pa mlandu o...
08/01/2026



Mayi wazaka 38, Esther James, amugamula kukakhala ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi kaamba kopezeka olakwa pa mlandu othyola ndi kuba katundu m'nyumba wa ndalama zokwana K149,000.

Bwalo la milandu ku Lilongwe ati linauzidwa kuti mayiyu adapalamula mlanduwu mu April m'chaka cha 2024, ku Area 36 munzinda wa Lilongwe.

Malinga ndi mneneri wa polisi ya Lilongwe, a Hastings Chigalu, maulendo atatu onse, mayiyu anathyola nyumba ya mayi wina ndikubamo katundu osiyanasiyana monga sugar, mafuta ophikira, zitenje komanso matilesi.

Olemba: Catherine Banda, Lilongwe



copied...

coming soon 🚨taverako pang'ono koma πŸ™ŒπŸ”₯
03/01/2026

coming soon 🚨

taverako pang'ono koma πŸ™ŒπŸ”₯


31/12/2025

Chaka chikutha samalan abale πŸ‘Š

Manchester United  apapa yabwela Kell Kay πŸ™ŒπŸ˜£
08/12/2025

Manchester United apapa yabwela Kell Kay πŸ™ŒπŸ˜£

19/10/2025

Sunday labwino kwa nose πŸ™

Phyzix  udolo wako unasefukila pano ophweketsa ose aja amakufunila zabwino kuli mulungu kunjaku πŸ‘ŠπŸ‘‘
26/09/2025

Phyzix udolo wako unasefukila pano ophweketsa ose aja amakufunila zabwino kuli mulungu kunjaku πŸ‘ŠπŸ‘‘

hip hop kugundana mitu 😴Gwamba  Olivia Media. Mikozi πŸ˜‚πŸ™Œ zaone nkhondo kuno
26/09/2025

hip hop kugundana mitu 😴

Gwamba

Olivia Media. Mikozi πŸ˜‚πŸ™Œ zaone nkhondo kuno

19/09/2025

Chakwera was chasing me in my Dream immediately i shouted Mutharika and he disappearedπŸ˜‚

19/09/2025

The MCP, UTM,PDP, and UDF are expected to hold a joint press briefing today in Lilongwe.

Follow WORLDstudios πŸ™

Tiponya ka fanta osadanda πŸ˜€πŸƒ
19/09/2025

Tiponya ka fanta osadanda πŸ˜€πŸƒ

Address

Chingwiri
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when WORLDstudios posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to WORLDstudios:

Share

//iconSize: [32, 32], //html: '' }) .bindTooltip(name, { //permanent: true, direction: 'bottom', //offset: L.point(12, 25), //opacity: 0.88, interactive: true }) .bindPopup(name); markersLayer.addLayer(marker); } function getMore() { if (gettingMore) { return; } gettingMore = true; var center = map.getCenter(); $.ajax({ url: "/vicinitysearch", data: { lat: center.lat, lng: center.lng, country: "MALAWI" } }) .done(function(data) { var added = 0; data.forEach(function(loc) { if (!locationIds.includes(loc.id)) { var mapLoc = {id:loc.id,lat:loc.latitude,lng:loc.longitude,title:trunc20(loc.name),popupHtml:loc.popupHtml,urlPath:loc.urlPath,pictureUrl:loc.pictureUrl}; locations.push(mapLoc); locationIds.push(loc.id); map._addMarker(mapLoc); added++; } }); }) .always(function() { gettingMore = false; }); } map._clearMarkers = function() { markersLayer.clearLayers(); } }); }, 4000); });