St. Patrick's Parish Choir 1

St. Patrick's Parish Choir 1 This is the main Choir for St. Patrick's Catholic Parish, Area 18 in Lilongwe Archdiocese, Malawi.

24/08/2026

Koma zikumveka kumeneko Mpingo!

Fr. John Kaliwamba ulemu wanu.

   As we celebrate the birthday of  πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚Wishing you abundant God's favour and many happy returns. Pitilidzani kutumikira...
16/08/2026





As we celebrate the birthday of πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚

Wishing you abundant God's favour and many happy returns. Pitilidzani kutumikira Mulungu mozipeleka muja muchitira.

Happy blessed birthday to youπŸŽ‚πŸ’πŸŽ‚πŸŒΉπŸŽ‚πŸŒΉ

 Happy blessed birthday to the Keyboard Man   πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚Wishing you God's favour and abundant blessings. Pitilidzani kusintha ...
29/07/2026



Happy blessed birthday to the Keyboard Man πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚

Wishing you God's favour and abundant blessings. Pitilidzani kusintha ma key muja muchitira kuti anthu avine basi! πŸŒΉπŸŽŠπŸ’πŸŽŠπŸ’

Enjoy the day mtchanaπŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚

29/07/2026

....Still in the season of celebrating the Golden Jubilee of St Patrick's Parish

 Kuli chaka kuno cha Mai  πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰79 years ago, mwana anabadwa ndipo adamutcha dzina la kuti   πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚. Ifetu timakunyadirani chi...
27/07/2026



Kuli chaka kuno cha Mai πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰

79 years ago, mwana anabadwa ndipo adamutcha dzina la kuti πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚.

Ifetu timakunyadirani chifukwa simutopa potilangiza. Munda ndi wawukulu koma antchito ndi ochepa. Pitilidzani kutumikira Mulungu kudzera m'mayimbidwe komanso ntchito zabwino zija mumagwira potumikira Mpingo.

May God continue keeping you safe and bless you abundantly.

Happy blessed birthdayπŸŒΉπŸŽ‰πŸŒΉπŸŽ‚

20/07/2026

Kumachezeratu kumeneko🌹πŸ”₯🌹πŸ”₯🌹πŸ”₯

20/07/2026
 Ili ndilo tsiku limene Chauta walipanga, tikondwe tikondwe chifukwa kuno kuli chaka Franco Magaleta Our   was born toda...
09/07/2026



Ili ndilo tsiku limene Chauta walipanga, tikondwe tikondwe chifukwa kuno kuli chaka Franco Magaleta Our was born todayπŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‰πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³.

We wish you more God's blessings and many happy returns as you celebrate this dayπŸŒΉπŸ’β€οΈπŸŒΉπŸ’. Pitilidzani kutumikira Mulungu mwa toto moyo kudzera m'mayimbidwe.

Happy blessed birthday πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚

Kwakoma ndi kuno lero!πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚David Banda komanso Adellah Katsala anabadwa lero. Zabwino zonse pa tsiku limeneli. Ambuye apit...
07/07/2026

Kwakoma ndi kuno lero!πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚

David Banda komanso Adellah Katsala anabadwa lero. Zabwino zonse pa tsiku limeneli. Ambuye apitilidze kukusamalirani pamene mukupitilidza kumutumikira kudzera m'mayimbidwe.

Happy blessed birthday to you twoπŸŽ‚πŸŽ‰πŸŽ‚πŸŽ‰πŸŽ‚

Address

Along Kamuzu Procession Road (M1 Road)
Lilongwe
P.O.BOX30006

Opening Hours

Monday 07:00 - 19:00
Tuesday 07:00 - 19:00
Wednesday 07:00 - 19:00
Thursday 07:00 - 19:00
Friday 07:00 - 19:00
Saturday 08:00 - 13:00
Sunday 06:00 - 15:00

Telephone

+265888880891

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when St. Patrick's Parish Choir 1 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to St. Patrick's Parish Choir 1:

Shortcuts

Share