Chosadziwa Z. Moyenda

Chosadziwa Z. Moyenda Public Figure
Giving you the best perspective
(2)

15/07/2026

Anthu omwe anamudyera DZOMBE 500million chaka cha 2019 sali kutali ayi. Ali mu Boma la DPP lomweri. Afufuzidwe ndipo tiwadziwe.

14/07/2026

So true

14/07/2026

Ma MP ena a DPP akuti DALITSO KABAMBE anadya Mfulumira ndipo abwerereso ku DPP


trendi
polit

14/07/2026

Alfred Gangata anangokhala OWUMA MUTU, bambo aketu ndi a Headmaster ku Primary School.


In the 21st Century, a normal person votes for policies that are tailored to transform the country, not short term solut...
13/07/2026

In the 21st Century, a normal person votes for policies that are tailored to transform the country, not short term solutions (pain killers).
Zowona chanzeru chikangokhala nsima basi?
Now people are struggling financially. Civil servants are receiving peanuts (pachipanda MCP kuyikapo transport and special allowance zikanakutherani bwanji kaya?). Anyway, tikudziwa you are angry with the current situation.
Koma simungayankhule. Mukuchita manyazi because you have learnt it in a hard way.

MCP ija osadzayitola maguy.

Ku state House kwayambika zibwana. Mmalo mogwira ntchito zowoneka pa ground, a Malawi awone ma Results enieni kuti ali n...
03/07/2026

Ku state House kwayambika zibwana. Mmalo mogwira ntchito zowoneka pa ground, a Malawi awone ma Results enieni kuti ali ndi President, Alimi agulidwe mbewu pa mtengo wabwino, basi busy kumujambula munthu ngati akugwira ntchito pamene pa ground penipeni a Malawi akulira.

03/07/2026

KALIATI AFUFUZIDWE, AKAYANKHE MAFUNSO KU PARLIAMENT

02/07/2026

Apa chair analowa nkalasi

Congratulations PRECIOUS KABAMBENew Landlord for Bwaila CONSTITUENCYDPP WAYIWONETSA NYENWA UKU
01/07/2026

Congratulations
PRECIOUS KABAMBE
New Landlord for Bwaila CONSTITUENCY

DPP WAYIWONETSA NYENWA UKU

"UNIVERSITY MUYIMVERA FUNGO" YATERO DPPPomwe a Malawi ambiri akupitira kulira ndimmene zinthu ziriri kamba koti DPP ikuk...
01/07/2026

"UNIVERSITY MUYIMVERA FUNGO" YATERO DPP

Pomwe a Malawi ambiri akupitira kulira ndimmene zinthu ziriri kamba koti DPP ikukanika kuyendetsa Boma, dzulodzuloli akwezaso School Fees ku school ya LUANAR. Apa nde apheratu makolo ovutika mkalewa. Ulimi sukuyenda kale bwino, fees ayitenga kuti makolo? Ma Salary ndi awaso akukanika kupereka kamba koti ndalama athera ma Private Trip komaso Campaign ya By-elections yomwe aluzaso konse.

Inde a Malawi amakonda Msima koma apapa or Msima yo ingakomeso??

Address

1
Lilongwe

Telephone

+972559424531

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chosadziwa Z. Moyenda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share