11/05/2026
*MUHIYI UYU OLONDIWA KUMAKA*
Amene mungamuwoneko Munthu uyu, Mundidziwitse ndi okuba ndi azinzake ena ake. Ndili ndi umboni wokwanira.
Akumanama kuti pali mwayi wa Bizinesi ya Mpunga ndi ma Bizinesi ena. Akalandira Ndalama Basitu! Sawonekanso. Pali enanso omwe andidandaulira. Mwina enanunso, anakufikaniponi. Akhala akubwera pa Shop panga ya ku Karonga, Malawi π²πΌ ya NSAYIWE INVESTMENTS. Nambala zawo, zikuwonetsa kuti akumapedzeka pedzeka cha ku Rumphi, Malawiπ²πΌ koma agwidwa ndithu. Ndipo abwenza zochuluka. Timapemphera mu Uzimu ndi mu Choonadi indee koma pali makhalidwe opusa ndi opepera, sitimatsekelera. MULUNGU sachitira CHIFUNDO Munthu WOPUSA.
Moti Nkhani ya ameneyi ndi Gulu lake ili ku Police ya Karonga, Malawi π²πΌ
Ndalama ngati yakuvutani kuyipedza, pewani kumapanga njila zopepera ndipo zoyikitsa Moyo wako ku Gahena.
Munganiyimbira pa nambala iyi +265 (0) 881 629 136