J4 Galu fanz

J4 Galu fanz Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from J4 Galu fanz, Comedy Club, KASUNGU, Kasungu.

27/06/2023

Eti anga andikwiila chifukwa ndinaisambitsa Madzi otentha yao ndalakwa chan pamenepo et gyzπŸ˜₯ follow J4 Galu fanz

GET WELL  πŸ’“πŸ’“πŸ’“πŸ˜₯
16/06/2023

GET WELL
πŸ’“πŸ’“πŸ’“πŸ˜₯

09/06/2023

Mpaka Abusa kupezeka ndi HIV ndiye nkhosa si bas tingoferatu πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
Like πŸ‘‡
J4 GJ4 Galu fanzuJ4 Galu fanzzJ4 Galu fanz

Koma zoona Mercy iweyo chilungamo IchiπŸ™ŒπŸ™Œ
06/06/2023

Koma zoona Mercy iweyo chilungamo IchiπŸ™ŒπŸ™Œ

06/06/2023

Kodi mamuna amasiya kuyamwa bere akafika zaka zingat? 🀣🀣🀣🀣

04/06/2023

Abale zoomwe ndaona ine dzulo ku shorprite ku blantyre abale zachilendo ndipo ine sinazione😭. Dzulo ndati ndikagule ndio mu shorprite chigao chakumadzulo ndithu Chama 3. Abale ndinadabwa chimkazi chowoneka bwino kwambili cholemela chagwada chikumuchondelela mamuna k*t amukhululukile amvekele" chonde Joe ndikhululukile sindizayambila" kmatu mamuna uja sikukanisisa kwake amvekele " choka galu iwe kukamwakwako wamva ndikangati ndikukhululukila, ndipo usandiyandikile ndikumenya sindimalimbana ndimahule. Abale mamuna uja atangonena izi mkazi ndiye analila misoz ikungotuluka ngati mvula yodzalila😭😭😭. Mene zimachitika izi mkazyo atayimisa galimoto yake potelopo. Ine nditangoyima kumangoonelela zomwe zimachitikazo kwinaku chitson chitandigwilaπŸ˜”. Mkazi anakwawa kukamugwila mwendo mamuna uja amvekele" chonde ndikhululukile inangokhala mistake " kma nyamaya uja anayankha mokwela amvekele" fuke ndisiye hule iwe ndati sindimalimbana ndimahule. Kenako nyamata uja anangomusiya mkazi uja Ali chigonele akulila iye kukakwela minbus wautali. Kenako inetu kumazifusa mafuso opanda mayankho ndimvekele " Asa zimwale ngat amene uja akumupanga chipongwe mkaz okongola kmanso olemela chonchi chifukwa chani?πŸ˜’. Kenako ndikumuona mkazi uja wadzuka kma kukasekula chiseko chagalimoto yake. Kma ine sinaphwekese Koma kumuthamangila kt ndikambilane naye nkhanπŸ˜…. Kenako k*t azikwela inetu ndamukodolekatu kunsana kenako ndikudabwaso munthu wina camera ilimmanja akundikodola kunsanaku amvekele " man kd muk*tani muk*tisokonezatu tikujambula video πŸ˜†. Anali achina manganya eti amajambula sewelo la tikufelanji πŸ€£πŸ˜‚πŸ˜†πŸ€£πŸ€£πŸ‘‰ followJ4 Galu fanz

Kumalawi mkokomad πŸ‘‰πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ‘‰ follow J4 Galu fanz
04/06/2023

Kumalawi mkokomad πŸ‘‰πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ‘‰ follow J4 Galu fanz

02/06/2023

πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ‘‰ follow J4 Galu fanz

Bambo mukumuona apayu ndimunthu wabwino kwambili wamuthandiza mzimayi kumuchotsa minga yomwe inamubaya karekare kuphaz w...
02/06/2023

Bambo mukumuona apayu ndimunthu wabwino kwambili wamuthandiza mzimayi kumuchotsa minga yomwe inamubaya karekare kuphaz wayesetsa kuyenda mzipatala km zosayenda muthakuona nokha m,mene zilili pachithumzipo πŸ‹οΈπŸ‹οΈπŸ‹οΈπŸ€£πŸ‘‰ follow J4 Galu fanz

Koma ana Ena πŸ‘‰πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ
31/05/2023

Koma ana Ena πŸ‘‰πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Address

KASUNGU
Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when J4 Galu fanz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category