27/12/2025
𝐙𝐢𝐥𝐢 𝐦'𝐦𝐚𝐤𝐨𝐦𝐨𝐦𝐮 𝐦𝐮𝐭𝐡𝐚𝐧𝐝𝐢𝐳𝐞𝐧𝐢 𝐦𝐚𝐠𝐚𝐧𝐢𝐳𝐨 𝐮𝐲𝐮
Very true but sometimes men can make u do worst things. Me and my husband have been married for 8 yrs now. I provide almost 85% of the house. Kumbuyoko I never complained thinking he will change some day. But no ndimazinamiza. He is the man who can not take care of my 2 daughters. He doesn’t even know kuti ana atsekera or atsegulira or kuti ana akhala number chani ku xool. He is always ku betting. He can’t even cook for himself even when am out ku field. If I go ku field ngati kuchipinda mzapeza mmene ku lili. M’bale pa sink zayamba kupanga ma fungus like….. he can’t even wash his boxer or mtakhalako bwanji ku field adzivala akudawo. He drives his elder brothers Car anamulemba ntchito Koma akapeza ndalama half will go ku betting kusangalatsa azimzake. I remember 2019 mtabereka mwana operation I was the one cooking for him bala lisanapole. I worked mpaka tsiku lopita kuchipatala and I even went to work 2 weeks after operation sindinadikire kuti lipole koz ana anga akanavutika. He is the guy oti if I tell him kuti ufa watha u will see akwawo abweretsa.. He can’t put effort p ifeyo. Chimandiwawa kwambiri ndipokhala ndi ana. Relationship yake ndi ana ake it’s zero. Zimndiwawa koopsya. He doesn’t smoke, drinking mwina once in times. Ine nthawi zonse ndimamupanga cover. Tikapanga chiganizo zokhuza family next day he will come saying mai Akuti zimenezo tisapange. There was. Time ndimkamuuza kuti tidalitse banja lathu. Then masiku atapitapo went ku maliro kwawo there with ma Ccta’s ake we were chatting saying nafe tidalitse banja lathu. Her elder ccta told me kuti amuna ako anachita kunena kuti ‘ Zopusa zake zaukwatizo apanga yekha’ since that day mtima wanga unakhumudwa was like oooo so if his ccta is telling me this….What else do they talk about? Am I forcing things. Since that’s day mnapanga chisankho chomapanga zitukuko zandekha. I don’t involve him anymore. Kusiyana mkosavuta Koma ine