22/09/2026
π₯πΆ ULEMU UPELEKEDWE KWA ANTHU OMWE ANAPANGA βVANITIβ β MALONEI KYZ πΆπ₯
Lero ndikufuna nditenge mwayiwu kupereka ulemu wapadera kwa anthu omwe adayika luso lawo pa nyimbo ya βVanitiβ ya Malonei Kyz. ππ½π₯
Nthawi zambiri tikamva nyimbo yabwino timangoyamikira artist yekha, koma kumbuyo kwa nyimbo iliyonse yabwino pali anthu ena omwe amagwira ntchito molimbika kuti nyimboyo imveke momwe imamvekera.
ποΈ Big Trump β Vocal Recording & Vocal Production
πΉ Branells β Beat Production
π€ Malonei Kyz β Artist, Songwriter & Performer
Kupanga nyimbo si masewera. Kugwira ma vocals bwino, kupanga beat yomwe ikugwirizana ndi artist, kulemba nyimbo, kupanga arrangement komanso kumaliza nyimbo ndi quality yabwino zimafuna luso, nthawi, creativity ndi teamwork. π―
Ichi ndi chitsanzo choti artist ndi producer akagwirizana bwino, akhoza kupanga project yomwe imakhala ndi quality komanso identity yake. π₯
Kwa ma artist onse omwe akufuna kutulutsa nyimbo zawo bwino, musamangoyang'ana kuti mukhale ndi beat basi. Yang'anani anthu omwe angamvetse vision yanu ndikuthandizani kusandutsa lingaliro lanu kukhala nyimbo yeniyeni. πΆ
Ku studio kwathu timagwira ntchito ndi ma artist omwe ali serious ndi music yawo β kuyambira beat production, recording, vocal production, mixing mpaka kumaliza nyimbo. ποΈπΆ
Ngati muli ndi idea ya nyimbo yomwe mukufuna kuti timange limodzi, tili ready kugwira nanu ntchito. π€π½π₯
π BIG TRUMP STUDIO
π© For bookings & projects, DM me.
Vaniti β Malonie Kyz π₯
Produced by Branells
Vocal Production/Recording by Big Trump
Big Trump Γ Branells Γ Malonei Kyz β teamwork imapanga music. ππΆ