25/04/2026
Katswiri Tarill
Wanted!
Mukumuona apayu ndi C I A. The guy behind audio production ya SingOdating. Ambiri mwankhala mukuyamikira beat ija komanso overall production ya audio. Mkulu waketu ndi ameneyu.
Mungakhulupirire kuti nyimbo yanga yoyambiliraso anapanga prod. ndi nkulu yemweyu in 2017? Nduziwa mwakhulupirira kale. 😅Anapanganso produce nyimbo zanga zina 5/6 ndikuyamba kumene kuimba komanso ndidakali ku secondary, HHI.
Chachikulu akulu akulu mangofuna (Wanted uja sopano) kuyamikira pa ntchito yomwe m’baleyu wagwira pa SingOdating.
Nyimbo yafakidwa Rajah okwanira iyi🔥
https://youtu.be/YQlaz8iCvwE