Mlakatuli kachepatsonga-stonneck matick

Mlakatuli kachepatsonga-stonneck matick Dont judge a book by its cover

Kuno ayamba๐Ÿ˜‰
18/10/2025

Kuno ayamba๐Ÿ˜‰

16/10/2025

Za anakubala izi๐Ÿ˜Š๐Ÿ™


16/10/2025

Hello guys mulibwanji Kodi muli ndi mafunso mumafuna mutandifunsa inbox Yanga ndi ya open kwa aliyense ndipo ndidzakuyankhani Moti mukhutire.

Zikomo Kaya mother's day yatha bwanji?

Happy mother's day to all responsible women all over the world.
15/10/2025

Happy mother's day to all responsible women all over the world.

14/10/2025

Yolakatulidwa ndi mlakatuli yokankha



14/10/2025

Ndakatuli ya anakubala iyi yokoma takaonerani ku YouTube guys link my comments box

Chikondi chanu mayi by Mlakatuli Mr Short Cut

Kuvala zovala zabwino kudzipopera perfume Koma uli osauka sizoti ukupanga Moyo wa fake,,,,sambani ,tchenani ,nunkhirani ...
14/10/2025

Kuvala zovala zabwino kudzipopera perfume Koma uli osauka sizoti ukupanga Moyo wa fake,,,,sambani ,tchenani ,nunkhirani musamachite kuoneka Ngati mavuto anu omwewu๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„

  Mkazi wa woyimba wa mdziko la America Akon, Tomeka Thiam, akufuna ndalama zokwana 100 million Euros  kuchoka kwa woyim...
13/10/2025



Mkazi wa woyimba wa mdziko la America Akon, Tomeka Thiam, akufuna ndalama zokwana 100 million Euros kuchoka kwa woyimbayu kuti asiyane naye ukwati patatha zaka 29.

Mkaziyu akufuna ndalamayi ngati chipuputa misonzi ponena kuti ngati mkazi anamuthandizira kwambiri woyimbayu kuti apeze chuma chake.

Koma bwalo la mdzikolo lomwe likuyendetsa nkhaniyi langopeza 10,000 US dollars mu akaunti ya Akon.

Pali kupenekera kuti chuma chambiri cha woyimbayu chili mdzina la amayi ake.

Izi zadzetsa zokambakamba pomwe ena akuti woyimbayu wachita dala kusintha umwini wa chumachi kuti akhaulitse mkazi wake pomwe ena akuti mwina Akon analibedi ndalama.

(Wolemba Jimmy Chazama)

13/10/2025

Hi everyone! ๐ŸŒŸ You can support me by sending Stars - they help me earn money to keep making content you love.

Whenever you see the Stars icon, you can send me Stars!

11/10/2025

Zosayenda๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„


11/10/2025

Enafe akutikalambitsa ndi maluzi omwewa koma sikuti ndife akale ayi๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿƒ๐Ÿƒ

Address

Chikwawa Road
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mlakatuli kachepatsonga-stonneck matick posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category