Anthu Osweka Mitima

Anthu Osweka Mitima Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Anthu Osweka Mitima, Arts and entertainment, Blantyre.

08/03/2024

Koma Kiss Alipo??😴

So sad😒🙌🏻Rest well  💚
02/03/2024

So sad😒🙌🏻
Rest well 💚

02/03/2024

Kell Kay verse in 🎼🎼
Inu monga Anthu Osweka Mitima line imakuwazani ndiitiyo🤪

🇲🇼VERSE🇲🇼
Ine zachibwana sikwenikweni/
Magwa mtchikondi zenizeni/
Ndipo ukabowa undimva pain/

Nde usandivutitse eeh
Pusitse

I don’t need bad energy in my life
Ndimagwila magobo to survive

If you wanna stay, Show me love
Ngati uzigulugusha, catch a bus

Mmmh tafumapo apa/
Sunakonzeke tafumapo apa/
Mmh nachilapa/
Zachikondizi nazilapa

Good vibes only wanted out here /
Uzindikonda za daily /
Give me love ena asilile /
Koma ukabhowa chikondi ndikwilile

Mchereeeee💪😁

02/03/2024

‼️Pena atiuze kuti "fight for what is yours". Pena amvekere "if it is yours you won't fight for it, it will definitely come to you". Lero chilimbikitso chivuta🙌😂. Ifenso tadzuka obalalika. GoodMorning everyone💥

01/03/2024

Amatikonda ndi Makolo athu omwewa basi😏🙌🏻

Mufuna muwauze kuti chani  😳
29/02/2024

Mufuna muwauze kuti chani 😳

Why this picture is trending now akuluakulu mwayisowa Ukali eti?

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anthu Osweka Mitima posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share