16/09/2025
ZISANKHO ZAYAMBA BWINO KU NDIRANDE
Olemba Enock Banda
Anthu ochuluka akukhamukila pa Ndirande Heathy Center kuzaponya voti yosankha Mtsogoleri wa dziko , phungu komaso khansala
Malingana ndi akuluakulu omwe akugwila ntchito pa malopa ati zonse zayamba bwino palibe chotsamwisa akumana nazo padakali pano.