DJ BOMBA

DJ BOMBA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DJ BOMBA, Arts and entertainment, Thekerani, Thyolo, Blantyre.

04/01/2026

Awawa nde ndi atate so, olo Joe ikon ndi mboni

30/12/2025

Ati amati chani? Anusaa!! Ga! Ga! Ga!
Mwazimveratu nokha apa

30/12/2025

December yu ndalamazo wonongani mwanzeru , kukubwera January uku

17/11/2025

Akuti anayimba nyimboyi amai wa Ali ndi nkhuku, Akufuna angomuthokoza

sangakane ai ndi yemweyo  IKK
23/09/2025

sangakane ai ndi yemweyo IKK

08/06/2025

Nyumba yowonetsera video show yapsa ku 50 pamene ana mawotha moto kuseli kwa video show Yi. Nkhani ikuti anawo amakonda kuwotha moto kuseli kwa video show ko Maka nyenga ya ngati inoyo(June), Ali mkati mowotha moto anawo anangozizimuka muto wagwila nawo shed ya video show Yi. Pomwepo anawo anathawa kusiya video show yo ikupsa, koma mwai katundu anali atachosamo ( kumalidza kuonera).

19/05/2025
18/05/2025

Abusatu mpaka kusiya kulalikila nkuyamva kuvina ,, koma Fred mw iwe uyankha mulandu

31/03/2025

A Police anathawa ndi nduna Ina inabwera pa yandika ground ndikuwasiya anthu akugendedwa kamba kowanamiza anthu kuti awapasa ndalama then kumgoliza galimoto lawo nkumapita Mpaka lalimoto limene ndinakwera ngati Dj linasekeredwa njira aaaaa

21/12/2024

With Umatha Daily – I'm on a streak! I've been a top fan for 3 months in a row. 🎉

21/12/2024

Kutentha kumeneku uzangozindikila kuti wakhonza mayeso a ku gahena, sukuzapsaso 😂😂😂😂😂

29/10/2024

KODI POLICE YA PA LINGAZI NDE KUTI AMANGOMANGA MA CELEBRATE OKHA-OKHA?

Address

Thekerani, Thyolo
Blantyre

Telephone

+265995602775

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ BOMBA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to DJ BOMBA:

Share