Chilungamo 24hrs daily

Chilungamo 24hrs daily Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chilungamo 24hrs daily, Arts and entertainment, Blantyre.

18/02/2024

Wa police akamalowa bank ngati akukatenga million koma ayi ndithu 🚢🚢🚢

Mau amodzi okha kwa mkulu uyu
11/11/2023

Mau amodzi okha kwa mkulu uyu

11/11/2023

Fact

Salary ya mphuzitsi wa primary sinakwane kupanga transport kuchoka ku sanje mpaka kukafika ku chitipa 😭

25/10/2023

Ndikufuna mkazi olimba mtima kuti athese banja langa landikwana 🚢🚢k50pin ilipo

18/10/2023

Penaso malemuwa mowa ndi akazi amaonjeza 😭😭😭

30/09/2023

Nanga apa munamizilaso kuti anakudyesa chokudya cha poison? 🀣🀣🀣

28/09/2023

Okongola Ali pa banja 🚢🚢🚢

28/09/2023

Kusaoneka bwino mwapindula nakotu 🀣🀣🀣 lero ndinu a madamu

25/09/2023

Kwatilani nafe tiziwanyenga akazanu kuti nanu mumve kuwawa momwe amamvela anthu enq mukamawanyenga akazao πŸƒπŸƒ

12/09/2023

Ndiye mulimwano mwa akadzi onenepa ku ntunda kokha ngati ntondo wa chigayo 😭😭

12/09/2023

Mkazi 58years
Mamuna 25years
Ankhoswe 19years

Inu agalu kwabasi 🀣🀣🀣

Khansala wa ku zolozolo akusegulila bridge ya 1 billion let's congratulate him
11/09/2023

Khansala wa ku zolozolo akusegulila bridge ya 1 billion let's congratulate him

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chilungamo 24hrs daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share