Mintchana

Mintchana 🚨 PROMOTE WITH US
Reach 100K+ people
DM β€œPROMO” now πŸ”₯
(10)

22/08/2026

Atati ma Ex anu aja aliyese akuponyereni 100k, mupezeka ndi ndalama zingati ?
πŸ€£πŸ€£πŸ’”πŸ’”πŸ™ŒπŸ™Œ

22/08/2026

kwatilani muzingotsonya nokha nokha minsewumuπŸ’”πŸ’”πŸ˜…πŸ€£πŸ™ŒπŸ™Œ

22/08/2026

Si anzanu onse omwe ayenera kudziwa komwe mumakhala, chonde. πŸ™ŒπŸ™Œ

22/08/2026

Ma boys tiyeni tilimbikire kuti zisafike size yomavala kabudula wa Mpira ngati Boxer please πŸ™πŸ€£πŸ€£πŸ’”πŸ’”πŸ™ŒπŸ™Œ

22/08/2026

Adona, boyfriend oti amavala kabudula wampila kupanga boxer mutan naye?πŸ§˜πŸΎβ€β™‚οΈπŸ˜Έ

The most important ceremony today: women and children handover TV remotes to their loving, caring, fertile, prayerful an...
21/08/2026

The most important ceremony today: women and children handover TV remotes to their loving, caring, fertile, prayerful and respectful men who have chosen to love their families and football, not other women.

Arsenal Vs Coventry City at 9 PM tonight. Kodi Arsenal itenganso?

21/08/2026

Kupatula " Avoid bush fire komanso School drop out" ndi Answer ina iti yomwe mumawinira ku Primary school?? 🀣🀣🀣

Kodi kali pa ndalama zingati aka??? πŸ₯ΊπŸ₯Ί
21/08/2026

Kodi kali pa ndalama zingati aka??? πŸ₯ΊπŸ₯Ί

21/08/2026

Kumauzana bwino bwino kuti ndafika pakwanu osati kumangoti tatuluka ngati ndine chiwanda πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

21/08/2026

Nzanga ukuwelengawe wadzuka bwanji

Address

Blantyre

Telephone

+265990464968

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mintchana posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Mintchana:

Shortcuts

Share