04/04/2020
Phyzix alusa
Pamene amalawi Rap Battle and Entertainment analemba post yoti mwachidule imati physix music yake imayenda kamba ka access Ku zinthu zomuthandzra otherwise samatha
Phyzix anatulukira yake ija kuika komenti yodziBakira k*ti EP yake ya Gamba season Chan kaya ak*ti ndiyabwno zedi iye wanenaso k*t muli ma punchline osamba,ma ryming wagwesa ngt Eminem waku America ndpo Wanenaso k*ti Chimbale(Album) chake ya Dododo ndye usayankhule ika ma full stop atatu.
Mpakana mkulu(admin) wa page ro wapepesa
Fuso nkumati dolo wa pageyo saphkidwa?
By admin
Like the to get more news