MAI MKULU MW

MAI MKULU MW Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MAI MKULU MW, Arts and entertainment, Blantyre.

07/08/2025

Life is what you make!!

07/08/2025

Uyu watha basi

24/07/2025

Zafika pa Kalikonse Mukaona

💥 MAI MKULU AKUTI:“Ladies, ndinu ana anga – koma mwatchulutsa chibwana!”Mwamuna akakuyitana — kaya for a date, kaya muli...
24/07/2025

💥 MAI MKULU AKUTI:

“Ladies, ndinu ana anga – koma mwatchulutsa chibwana!”

Mwamuna akakuyitana — kaya for a date, kaya muli pa relationship, kaya ndi nthawi yoti akuhopera — MUSAKANE!
Musapereke excuse!

Ndikuti musakane! Chifukwa chiyani?

Most of these men amakuyitanani tsiku limene ali ndi mtonyo — ndalama ilipo, fwalanga ilipo, mkwiyo wachepa.
Ukachedwa kapena kukana… amangoyendera kayitana kavula, then boom!
An indulgent night follows — ndalama yatha.
Tsiku limene wasankha kupita wekha kwa iye, umamupeza ali maluzi a nyooo, wakhuta ma chips, mang'ina ndi mowa.
Then we start saying “Satisamala”, “Ndi oshota, zaumphawiumphawi eee”, “Ndi chitsiru”...
Yet tinali ndi mwayi omupeza iye ali ndi ndalama zomwe anakatipanga nazo spoil. koma tinaona ngati potiyitana ali ndi kampeni kumphasa.
Most of men they invite a lady akakhala ali ndi money, koma ukasintha the plan, they lack patience, ndalama imeneyo imakhala kwa iwo yopanda plan, so they spend it unwisely.

🤭 MAI MKULU akunena: Mwamuna akakuyitana — tisachedwe kuwuyambapo! Nthawi zina amuna amasowa companu, osati chibwana.
💬 Kodi izi ndizoonadi kapena MAI MKULU wakunyasani?

👇 Ladies, comment “TIYENITU” if you agree!
👇 Gentlemen, defend yourselves below ⬇️

15/07/2025

😤 "Amuna ambiri samafuna mkazi wanzeru… amaona ngati akukhalira milandu! Amamutenga ngati ndi chiopsezo!" 😤

Koma MAI MKULU akunena izi:👇
Akazi amayenera kukhala ndi nzeru, osaopa kulankhula chilungamo. Ngati amuna ena akuona ngati ukulankhula kwambiri… ndiye kuti zomwe ukunena ndi zoona komanso zamzeru!

Amayi, tiyeni tikambirane:
🚩 N'chifukwa chiyani akazi anzeru amakhala osauka pa chikondi?
🚩 Kodi kuyankha mwanzeru kumachititsa kuti azikuwopa?
🚩 Kapena amuna akufuna mkazi amene amangosekelera zilizonse?

👇 Tag a woman who speaks her mind with pride!
💬 Men, tikumva: Is this true or are women twisting things?

🔥 COMMENT below: TRUE or LIE?

15/07/2025

Ana a ma 2 pin pambali
Mwayikumbukira iyi?

15/07/2025

🔥 MAI MKULU is Coming... Are You Ready? 🔥

“Moyo si wophweka… ndipo Mai Mkulu salankhula mopanda nzeru!”

A Reality Show Like No Other.
Secrets will be revealed.
Tears will fall.
Laughter will shake the village.
And Mai Mkulu will be watching… ready with her fire, her wisdom, and her judgment.

👀 Are you ready for raw truth, village drama, and real-life lessons?

📺 The countdown begins.
📍 Stay on this page.
💬 Tag your friend who loves gossip and wisdom at the same time.
👇 Drop a 🔥 if you’re ready to meet Mai Mkulu!

31/10/2024

Ngati muli ndi chakudya cha lero, tamandani Yawhe, anthu akubvutika kunjaku

31/10/2024

Imagine someone's husband busy praising someone's wife on daily basis on social media just bcoz the someone wife is a millionaire
Umphawi kupatsa utsilu mmh

29/10/2024

Atha kumaona ngati akukupusitsa, akukuyenda njomba, akukudyera but in true sense, akuzipusitsa okha bcoz they will lose munthu ofunikira, wa ulemu wake in u

28/10/2024

Inu muli Mbali iti?
Ya wife or Mother?

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MAI MKULU MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share