16/04/2025
Mwaswera bwanji agulu? pamene
sewero lanu la Nzotheka likhale likupitilira. Osaiwala kumvera wailesi ya Blantyre Synod nthawi ya 7:30 madzulo ano.
Mumenemu muli nkhani zaumoyo, zamaphunziro, za utsogoleri wabwino ndi zina zambiri.
Koma kodi lero nkhani yeniyeni yomwe iutse mapiri pachigwa ndiyotani???