Power-Emm

Power-Emm Music & stories

02/01/2024

Eee inu amenewo mbamu ngati muku pakulanso kkkkkkkk😂😂😂😂

08/10/2023

Zachisoni Bazukaa..😭😭😭😭😭RIP

07/10/2023

Komaditu ndikuononga zithu..mu tea kuthiramonso Milo aaaa..kumwanso mowa onse ,mutamwa tea othira Milo..

28/09/2023

Nonse mukuyakhula za John Tembo ...nyimbo nayi..

Mwainu,mwainu,mwainu ndindani sanachimwepo🎶🎶🎶🎶Ngati alipo agende🎶🎶
Nyimbo yabwera munthawi yake iyi..

27/09/2023

I have been broken too much ...mtima unalimba kalekale..🥰🥰🥰 ndikungofuna za Temporary 🎶🎶🎶🎶Saint-RealestRealest ubwera kudzakhala iweyo 🔥🔥🔥

26/09/2023

Za Temporary basi ...siza serious 🔥🔥Saint-Realest iyi mwampha 🔥🔥🎶🎶🎶

22/09/2023

Angel Gabriel inenso ndili pano mundiyendere🤸🤸

22/09/2023

Hustle sitisankha,Koma kodyera money🔥🔥

19/09/2023

Enanu mukungovutika nthiti yanu siili Ku Malawi Kuno🤸🤸

18/09/2023

Takula movutika Ife olo kuzimangirira sitingafe🤣🤣🤣

Address

Blantyre

Telephone

+265885589899

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Power-Emm posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Power-Emm:

Share

Category