15/03/2026
MONI ABALE NDI ALONGO
Dzina langa ndi Brighten Magalasi, Data Promotor wa Airtel Home Broadband ( HBB ) WI-FI ROUTER.
Kwa ma customer nonse amene mukufuna kugula Wi-Fi ROUTER, pamodzi ndi Data Bundle yomwe mitengo yathu ili motere:
1. 48200MWK with 30GB
2. 60000MWK with 65GB
3. 80000MWK with Unlimited
Abale amene muli ku South Africa, Amzanu akugulira okondedwa awo, moti sakuvutikanso kukaima pachulu kusaka Network π ya internet.
Wi-Fi ndi 30000MWK koma sitikulola munthu kugula popanda kugula ma DATA BUNDLE athu awaπ
4G IDU plan currently
18200=30 gb
30,000=65 gb
50,000=unlimite
Mlingo yonseyi ili ndi 100% Bonus for 6 months mukamapanga recharge.
Mukagula ndimapanga register, musanayambe kugwiritsa ntchito.
Zofunika popanga register:
1. National ID
2. Smart phone
3. Airtel number imene mumagwiritsa ntchito
4. My Airtel App, ngati mulibe ndimatha kukupangirani download.
5. SimCard ya New one yosapangidwa register
Mukafuna Product yathu mundipeze kwa Tengani.
For Call / Whatsapp: 0994353941