Zuze

Zuze Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zuze, Arts and entertainment, Malawi, Blantyre.

24/12/2024

(*LISSA BEAUTIFUL GIRL*)

PART 1

WRITTEN BY ZUZE

WHATSAPP 0602317133

Moyo uno ndiwovuta kwambili kwa atsikana ngati makolo awo amwalira ali ang'ono ndipo pachimenechi ena mwaiwo amayamba mchitidwe ogonana ali ang'ono kuti mwina azipedza chokudya sopo ndizina zotelo zokhuza moyo wawo ndipo mapeto ake amapezeka kuti atenga matenga komaso mimba mosayembekezera ndiposo ngati makolo amwalira ana ena amakhara ndi achibare amakolo awo omwe amawapanga zithu zankhanza kwambili zomwe zimawapangitsa kuyambaso zogonana komaso kupanga ziganizo zolakwika kwambili pamoyo wawo komano si onse omwe amapanga izi pakuti ena amalimba nazo mpaka amafika poziyimilira paokha moyo wawo mkumayenda ndithu

Lissa mamawa ngati uno wasamba wakutiko zikutheka bwanji iweyo kusamba ana anga asanasambe ndekuti wajayira pakhomo panga pano sichomcho mwana opusa iwe

Awa anali mawu amayi ake a Aisha omwe ndi mayi ake a Lissa ang'ono amakhara nawo chifukwa choti mayi ake omubeleka anamwalira ndipo analibe kuchitira mwina koma kukakhara ndi iwowo mzimayiyu anali muthu wankhanza kwambili chifukwa pakhomo tchito iliyonse amagwira ndi iyeyo mayi ake ang'onowo anali ndi ana awo atatu Aisha Princess komaso Samson anawa anali amatama kwambili muzochita zawo chifukwa amamuda kwambili Lissa komaso ku School anali ana opanda mzelu pamene Lissa anali tsikana wamzelu komaso owoneka bwino ndipo amuna ambili amamusilira kuphatikiza aphumzitsi ake

Lissa _____________ Amayi ndikupita ku school apapa mayeso ayandikira nde anatiudza kuti tilawire kwambili ndimkona ndalawira kusamba chomchi

Analakhura mawu awa akumwetulira posaganizira kuti ma Aisha anena kuti chani

Ma Aisha _____________ Ooooooooooh wati ku school anakuwuza kuti mulawire eti sichomcho kodi khomo lino walitenga ngati ndilako eti mayi ako mene amapita ku manda anakusiyira ndalama zoti uzidya eti sichomcho ukuzuka mkumapita ku school pomwe ana anga sanapite komaso wamwa tea pamenepo pomwe ana anga sanadye kodi iweyo ndi ana angawo yemw

Mongokumbutsana sinakwatirepo. Palibe amene anabwerako kwathu kuzapanga dongosolo lililonse kapena kundimveka engagement...
10/12/2024

Mongokumbutsana sinakwatirepo. Palibe amene anabwerako kwathu kuzapanga dongosolo lililonse kapena kundimveka engagement ring. nde muli ndi ufulu ondiuza zakukhosi kwanu koma mukandiuza zofoira ndifunsira ndekha. Ndanena ndanena😂


........
Your CCUTEY B

Kufana kwabwanji uku madala
10/12/2024

Kufana kwabwanji uku madala

Kell Kay all over.....🔥🔥🔥He deserves the respect❤❤❤❤
04/12/2024

Kell Kay all over.....🔥🔥🔥
He deserves the respect❤❤❤❤

😄
26/11/2024

😄

13/11/2024

Mtima wanga dekha

The fourth song from the late Martse's Truth Only Album will be out on Friday.  The title is 'Phula' featuring Charisma ...
30/09/2024

The fourth song from the late Martse's Truth Only Album will be out on Friday. The title is 'Phula' featuring Charisma 🎤

29/09/2024

And now, I understand why good mornings and good nights are important.

Morning greetings doesn't only mean good morning, it's implicitly means, "I remember you, and you're the first thought when I wake up",

and good night doesn't only mean good night, it's silently saying, "I still remember you and you're the last thought before I go to bed"

28/09/2024

Lord, I commit my academic journey into your hands.... Amen

27/09/2024

cheating is a choice, not a mistake. deleting messages so that the girlfriend can't see is already micro cheating. the bonding of friends that the girlfriend doesn't know is already cheating. why are you keeping lie to your partner? be honest. If you don't want that someone will stop from doing something, you would not enter in a relationship. You have to consider her side, you have to let her know what's you're going to do and what's your plans. You are in commitment not game.

It's easy to flirt, easy to cheat and easy to get what you want. But having someone who's truly sincere, honest and consistent, that's rare. So if you have them, keep them. Don't ever play with their heart and feelings. Because in the end you'll regret it.

Be honest with them. Tell them the truth no matter how painful or bad it is. You want to talked with your ex? Go tell them. Don't cheat. Just be real with them. No matter what happens, they will eventually know the truth. And if you'd tell them the truth and you're not lying, they will trust and understand you. Remember, truth hurts, but lies are wórse.
Facebook n Facebook Users

27/09/2024

Bwera by Waxy Kay is now out guys video x audio......

Link in the comment

27/09/2024

Kwa omwe mwasemphana chi nyimbo ichi cha Chacjesco please listen to it simuzakhumudwa.....

Link in the coment box

Address

Malawi
Blantyre

Telephone

+27695200808

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zuze posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share