19/04/2026
KODI MUKUDZIWA?
kodi mukudziwa kuti kupatula kukhala ndiwo pa tabulo NYEMBA zilinso ndi ubwino wa ukulu m'thupi mwathu? tikamadya NYEMBA timakhala tikuthandiza thupi, chifukwa zimagwira ntchito zingapo monga ;
1 - kuchepetsa chiopsezo chotha kudwala matenda a mtima.
- mu NYEMBA muli Fiber, Potassium, komanso antioxidants zomwe zimachepetsa kuthamanga kwa magazi.
- kudya NYEMBA kungakuthandizireni kupewa matenda a mtima
2 - NYEMBA zimathandizanso kuchepetsa matenda a khansa (e.g. prostate cancer, colon cancer, komanso khansa ya m'mabere)
3 - NYEMBA zimathandizanso kuti tisadwale kapena kuchepetsa matenda a Sugar (Type 2 Diabetes)
4 - NYEMBA zimathandizanso kagayidwe ka chakudya m'thupi (Digestive Health)..
DID YOU KNOW?
Beans are amazing for prevention and managing some diseases..here are a few:
- Heart disease: Bean's Fiber, Potassium, and antioxidants can help lower cholesterol and blood pressure.
- Type 2 Diabetes : beans' Fiber, protein can help regulate blood sugar levels.
- certain cancers: Beans contain antioxidants and fiber, which may help reduce risk of colon, breast, and prostate cancers.
Beans are also great for:
- Digestive Health: Fiber in beans supports healthy gut bacteria and prevent constipation.
- weight management: beans are filling and low in calories.
in Malawi, beans are a stable food.