The Daily Chilomoni

An entertainment platform aimed at recognizing and supporting local talent.It educates📢,informs📰 and entertains communities in Chilomoni, Sigerege, Mulunguzi, Khola, and surrounding areas.

19/08/2026

Ati nkulu ameneyi ndiwaku Center watiimilira kolandila ma Scorchers

Chikutamidwa m'ma group,ati nchoziwa zochita.Chinangoona kusiya mpira koma mchikatswiri ichi.Meet Dumisan Ntonya Chilomo...
19/08/2026

Chikutamidwa m'ma group,ati nchoziwa zochita.Chinangoona kusiya mpira koma mchikatswiri ichi.

Meet Dumisan Ntonya Chilomoni FC's goalkeeper trainer.

19/08/2026

Magogo ati ana a sukulu musiye kuba ....koma rrrrrrreeeeee!! Mmmh!!

Yatela🛬Welcome Scorchers🇲🇼🫡
19/08/2026

Yatela🛬Welcome Scorchers🇲🇼🫡

19/08/2026

🔥Kwabhebha ndiku Lilongwe kolandila ma Scorchers.

Ma neba mwakhala pati kodi?

Nkhani ndiyokuti akakutumizilani, inu musatumizile nzanu.Chifukwa munthu yo sanakupatse mphamvu yoti mufalitse."Kujambul...
19/08/2026

Nkhani ndiyokuti akakutumizilani, inu musatumizile nzanu.
Chifukwa munthu yo sanakupatse mphamvu yoti mufalitse.

"Kujambula, kutumiza, ndi kugawana makanema olawula a anthu popanda chilolezo chovomelezeka ndikosaloledwa.",MACRA yapeleka WARNING🙌

Happybirthday  vendor wakwa Nthukwa,Dalitso Nkhoswe.
19/08/2026

Happybirthday vendor wakwa Nthukwa,Dalitso Nkhoswe.

19/08/2026

Ana a Sigerege wa sakucheza awa, kwatuluka chi Trap song "Don't lie to yourself" yakwapulidwa ndi ana a trap Mandelah Slime ndi Gxrthyn

"Tipange ndalama kaye fame tilibe nayo ntchito singatidyese"- akutelo ma Slime wa.
Watch full video here👇
https://youtu.be/z6Cavb19XxQ?si=akCOvBnoSn_DwwMj

Nthutha Soccer Academy has one of the best youth setups in Chilomoni. The club is committed to developing young players ...
19/08/2026

Nthutha Soccer Academy has one of the best youth setups in Chilomoni. The club is committed to developing young players in every age group.

CHILOMONI LADIES FC INVITED TO MAYOR's TROPHY🏆Chilomoni Ladies FC, also known as the Lady Disciples, have been invited t...
19/08/2026

CHILOMONI LADIES FC INVITED TO MAYOR's TROPHY🏆

Chilomoni Ladies FC, also known as the Lady Disciples, have been invited to the Mayor's Trophy Bonanza!

Uku akhala akukumana ndima team ena omwe alowa nawo mu Bonanza yi monga:
FCB Nyasa Big Bullets Women,Kaso Ladies (Mulanje), Ekhaya Women,Mighty Wanderers Queens,Emmanuel Bullets (Chikwawa),Kukoma Ntopwa Women,Bangwe All Stars Women ndi ena omwe sanaziwike pakadali pano.

Zabwino zonse ma Ladies athu🔥🔥🔥🔥

Address

Chilomoni
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Daily Chilomoni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to The Daily Chilomoni:

Shortcuts

Share