Chayil Multimedia Malawi

Chayil Multimedia Malawi CMM is Malawi's Fastest Growing Online Advertising Brand 🇲🇼
(6)

11/06/2026

Uku nde kutembeleredwadi matsotsi ah 😂😂
Zigoli ziwiri, ma redcard awirinso pompo thiiiiiiiii!

11/06/2026

Mexico 1-0 RSA
'8
Zayambika

11/06/2026

On a second thought, lets all support South Africa. If they win the nation will rejoice and the attacks will stop.

Ma guy, 2 minutes inayake umunthu umafunika. Munthu akulirabe maliro a mwamuna wake wokondedwa mukamufunse funso lopusa ...
11/06/2026

Ma guy, 2 minutes inayake umunthu umafunika. Munthu akulirabe maliro a mwamuna wake wokondedwa mukamufunse funso lopusa ngati ilili? Ndinu oyipa mtima mwamva?

11/06/2026

Munthu wanzeru wasanja kale ma pulani opangira ndalama mu nyengo ino ya FIFA World Cup. Kuli kupanga ndalama za nkhaninkhani inu!

11/06/2026

Paja tonse tagwirizana kuti palibe wosapota South Africa Ku world cup, komabe uchipeza china chayipatsa payipi RSA

Guys, this trend is so alarming. Why are most Malawian music artists ditching Malawian girls for White women!Zinthu zija...
11/06/2026

Guys, this trend is so alarming.
Why are most Malawian music artists ditching Malawian girls for White women!

Zinthu zija zimakomatu chimodzimodzi Kaya ndiwe mkazi Kaya ndiwe mzungu Kaya ndiwe mkada!

Malinga Mafia Teddy Makadi ndi ProVoice Lameck tilankhuleni!

Chiphadzuwachi Dzina lake ndi Latoya ndipo zikumveka kuti chafunsira banja kamajeketeyo, yemwe ndi loya wodziwika.Izi zi...
10/06/2026

Chiphadzuwachi Dzina lake ndi Latoya ndipo zikumveka kuti chafunsira banja kamajeketeyo, yemwe ndi loya wodziwika.

Izi zikuchitika anthu atadandaula kuti katswiri wa zamalamuloyu akuchedwa kukwatira!

10/06/2026

World Cup nde ikuyamba mawa.
Ife tikuti Chikho ichichi ndi cha Portugal. Ronaldo needs this as an icing on the cake!

Bolako mzanuyu wabwera ndi pillow. Akakhala Prophet Shepherd Bushiri anabwerako ndi moyo wake wokha basi ndi kuyambirans...
10/06/2026

Bolako mzanuyu wabwera ndi pillow.
Akakhala Prophet Shepherd Bushiri anabwerako ndi moyo wake wokha basi ndi kuyambiranso kuswa mphanje!

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chayil Multimedia Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Chayil Multimedia Malawi:

Share