Kambodya

Kambodya [ACTOR] [COMEDIAN] [CONTENT CREATOR] [MUSIC PROMOTER] [INFLUENCER]

πŸ“© For business inquiries: [email protected]
(2)

19/05/2026

Kale lathu amkati bweretsa chimanga chako ndikukozele msewuπŸ’”πŸ’”πŸ™Œeeee matatizoo

18/05/2026

Bola Ana apano akamalila amawapatsa ice cream, Ife thaw imeneyo kungolira amatitengela pafup ndi bakha, avekere Luma luma πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

17/05/2026

kuluza ine waluza makina, aaa iwe takasambe uko makina anji Ali mbuuuπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

14/05/2026

Mkaz aliyese wagulu, sipalephela kukhala dolo mmodzi(admin) πŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

13/05/2026

Uvomela Bwanji k*ti umutumizila ndalama chosecho ulibe kalikonseπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

13/05/2026

4pin mpaka kufusa k*ti imalemba k*t ndan, aaa tangotumizani olo isochereπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

12/05/2026

Akaziwa amwene πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™ŒπŸ» Win Big Malawi Smile Media Group

12/05/2026

Kusungidwa sizithu achotselanji 4n yanga pa charge muli 5% mkuika po yawoπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

11/05/2026

Dolo ngat Ineyo ndikamvale zovala zosoketsa, kalichelo mmanja mudzina la chikhosweπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

11/05/2026

Munthu akamwalira timalira, akangoyelekeza kudzuka k*thawa kwake ko, kwenikwen timafuna ChanπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

10/05/2026

Mwana wa asing'anga naye banja likati limuvuteπŸ’”πŸ’”πŸ™Œ

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kambodya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share