GOD'S SAINT MUSICIAN, A MOTHER TO MANY. HELP TO THE NEEDY THROUGH SMALL BUSINESSES.
(5)
19/08/2026
Active member ulikuti? Ine phee kuganyu kwinaku ndikuswa ma plan 🤣
18/08/2026
Happy birthday Temwah ❤️❤️❤️❤️ Kapaseni maluwa ka byutifulu aka imweee🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
17/08/2026
Mama vungani 💰
17/08/2026
Ndi Monday liyambeni ndi mphamvu. Kulephera kwa last week kusabwezeretseni m'mbuyo.
16/08/2026
ANANDIBANA KUWAPASA ANTHU, ATI SI NDILI SERIOUS.CHONSECHO ANTHUNU NDAMENE SIMULI SERIOUS 🥰
NTCHITO 👇👇👇
Sandton
Stay in
Salary R4000
Off once a month
One child and 2 parents
16/08/2026
Munthu amumenya Kaye kokuba, nde ndimulowelenso live ah, asafike ponamizila kufa.
16/08/2026
Nkhani ya wakuba, uja anati ndine sister wake. Nangozitaya pena pake tisamupange promote satana. Ndungofuna ndidzacheze naye.
16/08/2026
Ma budget atsakulepheletseni kudya, moyo supanganyika 😋
Be the first to know and let us send you an email when Temwa Mkandawire posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.