Adziwi

Adziwi Music, Fashion, Art, Entertainment, News and Lifestyle
𝔞𝔪𝔞𝔩𝔞𝔴𝔦
(1)

THUPI LA MALEMU BRIAN BANDA LIZAYIKIDWA M’MANDA LOLEMBA—Brian Banda, amene anali mkulu wakale wa MBC, adzaikidwa m’manda...
08/08/2026

THUPI LA MALEMU BRIAN BANDA LIZAYIKIDWA M’MANDA LOLEMBA

—Brian Banda, amene anali mkulu wakale wa MBC, adzaikidwa m’manda Lolemba, pa 10 August 2026, ku M’banda Village, Chileka.
💔🕊️

Mkulu wa wailesi ya boma ya MBC, Brian Banda, wamwalira. Banda, yemwe wangosankhidwa pa udindowo posachedwapa, wamwalira...
08/08/2026

Mkulu wa wailesi ya boma ya MBC, Brian Banda, wamwalira. Banda, yemwe wangosankhidwa pa udindowo posachedwapa, wamwalira maola angapo apitawa mu mzinda wa Blantyre.

Iwowatu amadziwika bwino kamba ka luso lawo lofunsa mafunso maka pa nthawi yomwe anali mu uwulutsi wa mawu ku wailesi ya Capital komanso ku Times.

Zambiri za imfa ya a Banda, tikupatsirani. Mzimu wawo, uwutse mu mtendere. 💔🕊️

Jude Okoye’s Elder Brother, Henry, Speaks on the Psquare Feud: “Jude Is Not a Good Person✍️Henry Okoye, the elder brothe...
08/08/2026

Jude Okoye’s Elder Brother, Henry, Speaks on the Psquare Feud: “Jude Is Not a Good Person✍️

Henry Okoye, the elder brother of Psquare stars Peter and Paul Okoye, has spoken about the long-running family issues involving his brothers and their elder brother, Jude Okoye.

Henry said he was one of the people who supported Peter and Paul when they were starting their music career. According to him, he helped them financially and even took them to performances when they were still struggling.

He explained that the family has eight children, six boys and two girls and said that when Peter and Paul started music, they were looking for sponsors. He claimed Jude was not involved at that early stage.

Henry said the family initially saw Psquare’s success as a family achievement, although everyone knew Peter and Paul were the ones who owned the music group.

He also said Jude later became their manager after the family agreed to let him take the position, despite their mother reportedly having concerns about Jude’s character.

According to Henry, things started changing as Psquare became more successful. He claimed Peter and Paul gradually became distant from the family, and they did not initially realize that Jude was part of the problem.

Henry made a strong statement about his brother, saying, Jude is never a good person. He’s my brother, but he’s very bad. I’m telling you the truth

He also revealed that he and Jude have not spoken for almost two years. Henry said that even when he was hospitalized for two months last year, Jude allegedly never called to check on him, while Peter and Paul regularly called.

Henry also claimed that their younger sister is struggling in Lagos and said she has not received enough support from the family. However, he acknowledged that Peter has been trying to help her

Speaking about Paul, Henry said he was surprised by how much Paul’s character has changed over the years. He even wondered aloud if there could be some spiritual influence involved, but admitted that he had no proof and could not confirm it.

These are Henry Okoye’s claims and personal account of the family situation.

UNIMA GRADUATE KILLS 17 YEAR OLD EX GIRLFRIENDMnyamata wina yemwe anali ophunzira wa ku University of Malawi ndipo wapan...
05/08/2026

UNIMA GRADUATE KILLS 17 YEAR OLD EX GIRLFRIEND

Mnyamata wina yemwe anali ophunzira wa ku University of Malawi ndipo wapanga graduate pompano wapha mtsikana wazaka 17, dzina lake Shingirai, pamalo otchedwa Tholo, omwe ali mu dela lotchedwa Kazembe ku Zomba City.

Shingirai, dzulo amachoka mtauni momwe Mai ake amapanga business. Anali ndi mzake ndipo akuyandikila pa Tholo pa, anadabwa kuwona mnyamata yi yemwe anasiyana naye chibwenzi pa kanthawi akumudikila.

Ndiye anamuuza kuti ndidikile tikambirane zomwe Shingirai anakana. Ndiye mnyamata yu anayamba kumumenya mtsikana yi, kenaka kutulutsa mpeni ndikumubaya pa chest kawiri kenaka ndikuthawa.

Shingirai amakhala kwa Chikanda mu City yomweyi ya Zomba ndipo Bambo ake omwe amagwira ntchito nthawi yayitali ngati prison warderer anamwalira kumayambiliro a Chaka chino.

Programme yamaliro ikunveka kuti ndiwonyamula ndipo akayika mboma la Thyolo

Kulakwa Woyimba wotchuka wa dziko la Nigeria R***r yemwe wafika dziko muno kudzayimba pa chiphwando chamayimbidwe chomwe...
02/08/2026

Kulakwa

Woyimba wotchuka wa dziko la Nigeria R***r yemwe wafika dziko muno kudzayimba pa chiphwando chamayimbidwe chomwe chidakonzedwa ndi Gwamba, anthu awupandu amubera phone yake pa BNS show itagotha.

Pakadali pano kafukufuku ali nkati kuti apeze yemwe waba phone ya international artist uyu.

Paja zimayamba choncho but 5 years is enough
02/08/2026

Paja zimayamba choncho but 5 years is enough

Happy birthday Crispy Malawi AKA spenalditho 🍄brrrr
01/08/2026

Happy birthday Crispy Malawi AKA spenalditho 🍄brrrr

Chinthu chija chafikadi mu DZIKO muno 🙏
31/07/2026

Chinthu chija chafikadi mu DZIKO muno 🙏

Ndi Njonda mayi ameneyi
30/07/2026

Ndi Njonda mayi ameneyi

Kokudaida small wifey unakadekha Kaye osati wapangadzi😔💔
28/07/2026

Kokudaida small wifey unakadekha Kaye osati wapangadzi😔💔

Address

Blantyre

Telephone

+265212967032

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Adziwi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Adziwi:

Shortcuts

Share