Yusuf Bamus

Yusuf Bamus I am distinguished Malawian poet celebrated for his profound works in Chichewa and Arabic.

My poetry reflects a unique blend of cultural and linguistic depth, capturing themes that resonate with local and global audiences alike." My poetry reflects a unique blend of cultural and linguistic depth, capturing themes that resonate with local and global audiences alike.

Big shout out to my newest top fans! πŸ’Ž Ibrahim Abuh Khareed, Stanley Elson, Patrick Kachingwe, Zainab MuyereDrop a comme...
18/03/2025

Big shout out to my newest top fans! πŸ’Ž Ibrahim Abuh Khareed, Stanley Elson, Patrick Kachingwe, Zainab Muyere

Drop a comment to welcome them to our community, fans

Maloto Alero.Eti ine Kulota nditalandira tenifolo kuchokera koooomweEhe!. Kunyumba yachifumu. Akuti a Yusuf Bamusi mwatu...
23/02/2025

Maloto Alero.
Eti ine Kulota nditalandira tenifolo kuchokera koooomwe
Ehe!. Kunyumba yachifumu. Akuti a Yusuf Bamusi mwatulutsa ndakatulo ya maloto alero. Tipatseni link Amfumu akufuna amvere
Nthawi yomweyo link kuti phaa!: https://youtu.be/uTw2A_p3iAQ

Kamvereno ku Youtube. Koma osaiwala kutipanga support.
Chaka chino kukununkhira Album.

Mndakatuloyi, muli ena mwa mavuto atsiku ndi tsiku omwe a Malawi ife a Malawi tikukumana nawo. Tipemphe Mulungu atithandizo pa moyo wathu padzikoli.

YATULUKATU ⚠MALOTO ALEROPezani ndakatuloyi potumiza K1,000 kapena kuposera apo ku 0991121411 | 0880139491 | 990604 Natio...
17/02/2025

YATULUKATU ⚠

MALOTO ALERO
Pezani ndakatuloyi potumiza K1,000 kapena kuposera apo ku 0991121411 | 0880139491 | 990604 National Bank of Malawi (NOORDIN CASSIM)

YUSUF BAMUSI OFFICIAL YOUTUBE CHANNELKwa nonse amene mumakonda Ndakatulo zanga. Ndipangeni support popanga subscribe ku ...
11/02/2025

YUSUF BAMUSI OFFICIAL YOUTUBE CHANNEL
Kwa nonse amene mumakonda Ndakatulo zanga. Ndipangeni support popanga subscribe ku YouTube Channel iyi yomwe ma project onse azitulukira kupita mtsogolo muno.

https://www.youtube.com/

Osaiwala kuti Lowerukali, 6:00 Madzulo kukutuluka ndakatulo mutu wake MALOTO ALERO yomwe mtengo wake ndi K1,000 yokha basi.

M***a kuguliratu ndakatuloyi potumiza K1,000 kapena kuposera apo ku 0991121411 | 0880139491 | 990604 National Bank of Malawi (NOORDIN CASSIM)

Yusuf Bamusi is a distinguished Malawian poet celebrated for his profound works in Chichewa and Arabic. His poetry reflects a unique blend of cultural and linguistic depth, capturing themes that resonate with local and global audiences alike.

10/02/2025

Live performance iyi ku Muslim Arts Awards. Njoyaniko ndakatulo yapamwambayi

MALOTO ALEROMu ndakatuloyi, Yusuf Bamusi akufotokoza nkhani zomwe zikukhudza moyo wathu watsiku ndi tsiku. Ndakatuloyi i...
10/02/2025

MALOTO ALERO
Mu ndakatuloyi, Yusuf Bamusi akufotokoza nkhani zomwe zikukhudza moyo wathu watsiku ndi tsiku. Ndakatuloyi ituluka pa 15 February, 2025. Nthawi ya 6 Koloko madzulo.

M***a kuguliratu ndakatuloyi potumiza K1,000 kapena kuposera apo ku 0991121411 | 0880139491 | 990604 National Bank of Malawi (NOORDIN CASSIM)

31/12/2023

Abale ndi Alongo

Mulibwanj kulikonse komwe muli?😊

Ine mlakatuli wanu *Yusuf Bamus * munandipanga nominate pa MBC entertainers of the year pa ndakatulo ya *zaimfa* *yanga*

Sitinachite bwino chifukwa sitinatenge Award imeneyi

Ndikuthokozen kwambir pantchito yomwe munaigwila yondivotera, mwagwira ntchito yotamandika kwambir aliyense payekha payekha amve kuthokodzedwa..nthawi zonse ndibwino kuvomeraza mwachangu zimene Mulungu watilembela 😊

Regards
Yusuf bamusi(the poet)

29/12/2023

Vote for Za Imfa Yanga by Yusuf Bamusi as the Best Poem of the Year in MBC Entertainers of the Year.
Dial *364 #
Select Language
Select 1
Select 3 (Poem of the year)
Select 2 (Za imfa yanga)

Ndi K50 yokha bas

Malire ndi pa 30 December

Iyiyi Ndi nthawi ya bwino yomuvotetera m'bale wani Kwa amene simunatero

28/12/2023

Vote for Za Imfa Yanga by Yusuf Bamusi as the Best Poem of the Year in MBC Entertainers of the Year.
Dial *364 #
Select Language
Select 1
Select 3 (Poem of the year)
Select 2 (Za imfa yanga)

Ndi K50 yokha bas

Malire ndi pa 30 December

14/12/2023

The Health of Married man depends on His Wife.

Choose wisely..

Koma Ndi kovota

Address

Limbe
Blantyre
0000

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Yusuf Bamus posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Yusuf Bamus:

Share

Category