13/10/2026
50 billion gang anthu akukamba za zeze kingston tsiku ndi tsiku chagawa ndalama ku show
Nde ena akuti milandu imeneyo ife tikuti ndizoona malamulo akutelo koma asagwile ntchito pa zeze yekha andale aja akumaponyaso ndalama aja muwamange