11/05/2026
Nzotheka makolo kuthesa ubwenzi koma nkovuta kuthesa chikondi....
Or
Muyamba bwanji kutheka ubwenzi chikondi chilipo????
Kapena
Nkhani zawanthu okondana nzovuta kuzilowelera....
Umazapusa pamawa......