Malawi Nasheed Network

Malawi Nasheed Network Malawi Nasheed network -
Inspire, Unite & promote Islamic arts

03/05/2026

QIYAMUH DALEELUH QD POEM PRESENT

NKACHABE
POEM By Shukran Vakhan
Coming soon

28/04/2026

Chilungomotu Ichii

18/03/2026

Abaya By Poet Kinanah Jannah
Simmene kulili

05/03/2026

Uthenga

28/02/2026

Uyuyu Ndi Biläl akutulutsa Ndakatulo Yotchedwa TSOKA lero

02/02/2026

Ambiri akuitama Ndakatulo iyi Kuti yawayankhulira
Muzitembelera Anthu Akwanu By Allie Hozzar Seleman

02/02/2026

Osamangodyatu zilizonse kumeneko mudya Nazo chibudu,
Uyu ndi CheYinoyino Nasheed yake yatsapano akuti

07/12/2025

New Poem Alert ✨

I'm Me By Poet Kinanah Jannah

07/11/2025

Wanzeru anati: zinthu zinayi ndi zabwino, koma pali njira ina yomwe imakhala yabwinoko:

Kukunena choonadi ndi kwabwino kwa olemera, koma kwa osauka n’kwabwinoko.

Kudzichepetsa (manyazi) ndi kwabwino kwa akazi, koma kwa amuna n’kwabwinoko.

Kulapa ndi kwabwino kwa okalamba, koma kwa achinyamata n’kwabwinoko.
Chilungamo ndi chabwino kwa aliyense, koma kwa olamulira n’kwabwinoko.

18/10/2025

Mwana wa mkazi wa Chisilamu, niqaab ndi mphatso yochokera kwa Allaah.
Si chovala chokongoletsera kapena chofuna kupezera ma likes, koma chitetezo cha ulemu wako ndi chizindikiro cha kulemekeza Mulungu wako.

Pamene ena akugwiritsa ntchito TikTok kuvina ndi kudzikongoletsa seeking attention ya Anthu osakhala Attention ya Allaah, iwe khala wosiyana ndi iwo chifukwa wasankha kusunga khalidwe.
Koma ngati niqaab yawoneka pa ukuvina, zimachotsa tanthauzo lake.
Ulemerero wa niqaab si mmene anthu amakuwonera, koma mmene Allaah akukuonera.

Kuvina pa TikTok, ngakhale mutaphimba nkhope, kungakoke chidwi cha amuna ndi kusokoneza omwe amaona nyasizi.
Zimenezo zimakhala chiopsezo cha fitnah, ndipo sizigwirizana ndi umunthu wa mkazi wosiririka.
TikTok imakopa chidwi cha anthu, koma osalola chidwi cha anthu kuchotsa ulemu wako.

Choncho, musachite kuti anthu akukonde,
koma muchite kuti Allaah akukonde. Musapereke Mpata kwa Anthu Omwe akusakasaka njira zotukwanira akazi ovala motere kuti ndimongobisalira koma ndi Ashawuwo.

Ulemerero wa mkazi si thupi lokha kapena maonekedwe,
koma mu khalidwe, mtima, ndi kulemekeza malamulo a Allaah,

Khalani chitsanzo, osati chidwi.
Khalani ofatsa, osati masewera mukuchitawa
Khalani ndi niqaab yomwe imalemekezedwa ndi anthu komanso imavomerezedwa ndi Allaah.

May ALLAH the Almighty Guide us all

Kinanah Jannah.

WASSALAM ALAYKUM WARAHMATULLAH WABARAKATUH

Address

Blantyre

Website

http://fb.com/stars

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Nasheed Network posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share