Single mother/life motivation by mama AngelGabriella chiyabwe

Single mother/life motivation by mama AngelGabriella chiyabwe I wanna to encourage people to not give up in life no matter challenge they face

07/07/2025



Apolisi ku Mwanza ati akusunga mwana yemwe dzina lake ndi Letisha Kampeni amene akuganiziridwa kuti watayidwa ndi mayi ake.

Malinga ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Mwanza, a Hope Kasakula, mwanayu akungokwanitsa kufotokoza kuti amachokera m'mudzi mwa Mkando m'boma la Mulanje ndipo ali standard 4 ngakhale akulephela kunena komwe mayi ake apita.

A Kasakula apempha akubanja la mwanayu kuti akamutenge ndipo agwiritse ntchito nambala izi polumikizana ndi apolisi: 0999343828 kapena 0884112145

Wolemba: Catherine Alumando, Mwanza.

07/07/2025

Love you kids ladies always

16/10/2024

Kukhalat single parent sikuphai

16/10/2024

If your malawian Nde muli Ndi sikana olo Zimai akuzuzika kulera I'm a yekha mwamuna anakanira inbox .Tithandizane girl

16/10/2024

Welcome ladies and everyone out theirrr.lets fight battles that single mothers facee..in different ways

19/06/2024

Hello fellow single mother out their..let gather here an talk for few minutes

Will do some fundraising for single mother who lacks some basic need

29/12/2023
Happy always and be free to be happy
03/05/2023

Happy always and be free to be happy

Address

Thyolo
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Single mother/life motivation by mama AngelGabriella chiyabwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share