21/05/2026
Kwainu ndi Emmie Deebo koma kwaine ndi Emily Zintambila Phiri ...wa Praise team wanga uyu ..osanganiza zambiri
Nditanva kuti mwanayu akufunika New Manager ndachiona chinthu chofunika kuti uyu ndiyende naye
Koma chomwe chandipangitsa kuti mpaka mtumiki wa Ambuye asankhe mwanayu ndichakuti mwanayu ndi Role model wanga kumbali yakavalidwe Emily kulibe size yake