Low Profile Malawi

Low  Profile  Malawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Low Profile Malawi, Art, London.

Komatu muli mdalitso shaaaaaa!!!! Mukuona bwanji?
18/12/2025

Komatu muli mdalitso shaaaaaa!!!! Mukuona bwanji?

18/12/2025

Let's be honest!!! Mukuona ngati akupanga apolisi zi ndioona kapena za bodza za anthu 6 awamangawa?

Three Malawian Winners at the Zikomo Africa AwardsTemwa - Best ArtistEmmie Deebo - Best Female Artist, Southern AfricaSh...
18/12/2025

Three Malawian Winners at the Zikomo Africa Awards

Temwa - Best Artist
Emmie Deebo - Best Female Artist, Southern Africa
Shepherd Bushiri - Philanthropist of the Year

Congratulations ๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘

Most awards have gone to Tanzania, Zambia and DRC

17/12/2025

Amuna nde amangodya nkumapita pano ndufuna wa serious mamuna andikonde abwere ku UK ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ง ndizizakhala naye.

Ngati mukufuna muyankhuleni Connex

17/12/2025

Tawonani Tawonani, mpwerere pa mpunga wa gulu.

Wa thululu zonga za mango ali mpwii, mpwee atazimbidwa

17/12/2025

Two prominent legal practitioners have criticised the Malawi Police Service for taking six suspects in the murder of Kamuzu University of Health Sciences lecturer and Queen Elizabeth Central Hospital doctor, Dr Victoria Bobe, to the scene of the crime in Blantyre, describing the move as unprofessional and potentially prejudicial.

During the visit earlier today, the suspects narrated how they allegedly committed the crime at the deceased's house in Chigumula.

But lawyer Sylvester Ayuba James through his page said the exercise amounted to โ€œtheatricsโ€ rather than a proper investigation, warning that such actions undermine the presumption of innocence guaranteed to suspects before trial.

He argued that investigators appeared to be seeking public validation instead of focusing on legal standards required in court.

James stressed that questioning police conduct does not amount to condoning the murder, noting that while Dr Bobeโ€™s death was tragic, investigative institutions must act with care and restraint.

Another lawyer, Khumbo Soko, echoed similar concerns, stating that investigators should not โ€œplay to the galleryโ€ but focus on presenting a strong case before the courts.

He said police work must be done quietly and professionally to avoid creating loopholes that defence lawyers could exploit.

Soko warned that courts are guided by evidence and procedure, not public emotion, and that poorly handled investigations risk cases being dismissed.

The six suspects remain in custody as investigations into Dr Bobeโ€™s murder continue to bring to book two more individuals.

Aka ndi kachiwiri kumva nkhani iyi. Atsogoleri a DPP muli kuti? Ndipo n'chifukwa chiyani mukuzilekelera izi? From my inb...
17/12/2025

Aka ndi kachiwiri kumva nkhani iyi. Atsogoleri a DPP muli kuti? Ndipo n'chifukwa chiyani mukuzilekelera izi? From my inbox:

Bwana Kenani chonde tidzudzulireni anyamata awa a DPP. Afika pomangogawana malo panja pa mipanda pa anthu. Imagine they came ku nyumba kwanga only to tell me kuti panja pa mpanda wanga akugawanapo malo omangilapo ma shop and yet nyumbayo takhalamo zaka and izi sizinachitikepo. Mpaka ndinawauza kuti zimene akupangazo sizinachitikepo even nthawi ya dpp or mcp , only to be answered kuti ino ndi nthawi yawo and they went ahead kugawana malo panja pa mpanda wanga . Funny thing ndikundiuza kuti inenso andigawile malowo koma ndawakanila. Mafumu adziwitsidwa komanso a housing and a city onse adziwitsidwa and onse akunena kuti zimene zikuchitikadi sizoyenela. Koma palibe amene wachitapo china chilichonse kuti achotsedwe pa malopo.

Bambo wina wa zaka 45 ali m'manja mwa apolisi ku Chitipa pomuganizira kuti wapezeka ndi chamba popanda chilorezo.Mneneri...
17/12/2025

Bambo wina wa zaka 45 ali m'manja mwa apolisi ku Chitipa pomuganizira kuti wapezeka ndi chamba popanda chilorezo.

Mneneri wa polisi ya Chitipa Sub Inspector Gladwell Simwaka wati bamboyu ndi David Kayinga ndipo wamangidwa usiku wapitawu.

Iwo ati anthu akufuna kwabwino adadziwitsa apolisi kuti mkuluyu amagulitsa chamba ndipo apolisi adapita komweko ndikumupeza ndi ma kilogram 20 a chamba-chi ndipo adakazulaso chamba chomwe mkuluyu amalima kumunda kwake.

Mkuluyu ndi wa m'mudzi mwa Mwakalama kwa mfumu yaikulu Mwaulambia ku Chitipa.

ZINA UKAMVAUsiku wa dzulo ma bus 9 a kampani ya Buscor aotchedwa ndi anthu omwe sakudziwika ku Mpumalanga ku town ya Bab...
17/12/2025

ZINA UKAMVA

Usiku wa dzulo ma bus 9 a kampani ya Buscor aotchedwa ndi anthu omwe sakudziwika ku Mpumalanga ku town ya Baberton mdziko la South Africa..

Izi zikudza pa nthawi yomwe pali kusamvetsetsana ndi anthu oyendetsa ma Taxi.

Kodi mutakhala lawyer wake mungati chani mu khoti pomupanga defend nkulu akuganizilidwa kuti anapanga pull trigger yu.
17/12/2025

Kodi mutakhala lawyer wake mungati chani mu khoti pomupanga defend nkulu akuganizilidwa kuti anapanga pull trigger yu.

๐๐ž๐š๐œ๐ž ๐Ž๐ฏ๐ž๐ซ ๐๐จ๐ฅ๐ข๐ญ๐ข๐œ๐ฌ: ๐Š๐š๐ฌ๐ฎ๐ง๐ ๐ฎ ๐‹๐š๐ฐ๐ฆ๐š๐ค๐ž๐ซ ๐‚๐ก๐ข๐ค๐จ๐ง๐๐ข ๐Š๐š๐ฆ๐ฉ๐š๐œ๐ก๐ข๐ค๐ž ๐‚๐ก๐ข๐ฌ๐š๐ฅ๐ž ๐ƒ๐ซ๐จ๐ฉ๐ฌ ๐‚๐š๐ฌ๐ž,๐๐ซ๐ข๐จ๐ซ๐ข๐ญ๐ข๐ณ๐ž๐ฌ ๐ƒ๐ž๐ฏ๐ž๐ฅ๐จ๐ฉ๐ฆ๐ž๐ง๐ญ Lilongwe,Malawi In ...
17/12/2025

๐๐ž๐š๐œ๐ž ๐Ž๐ฏ๐ž๐ซ ๐๐จ๐ฅ๐ข๐ญ๐ข๐œ๐ฌ: ๐Š๐š๐ฌ๐ฎ๐ง๐ ๐ฎ ๐‹๐š๐ฐ๐ฆ๐š๐ค๐ž๐ซ ๐‚๐ก๐ข๐ค๐จ๐ง๐๐ข ๐Š๐š๐ฆ๐ฉ๐š๐œ๐ก๐ข๐ค๐ž ๐‚๐ก๐ข๐ฌ๐š๐ฅ๐ž ๐ƒ๐ซ๐จ๐ฉ๐ฌ ๐‚๐š๐ฌ๐ž,๐๐ซ๐ข๐จ๐ซ๐ข๐ญ๐ข๐ณ๐ž๐ฌ ๐ƒ๐ž๐ฏ๐ž๐ฅ๐จ๐ฉ๐ฆ๐ž๐ง๐ญ

Lilongwe,Malawi

In a move hailed as a testament to leadership and a commitment to unity, Honourable Chikondi Luv-christ Chisale , the Member of Parliament for Kasungu Central, has announced the withdrawal of a case involving him and the State Second Vice President, Honourable Enoch Kamzingeni Chihana who is also the leader of Alliance for Democracy(AFORD).

The case stemmed from incidents during the recent campaign period, including the damaging of Honourable Chisaleโ€™s vehicle and the alleged theft of funds and campaign materials.

The decision, explained Honourable Chisale, comes after careful consideration and consultation with community leaders. He acknowledged the gravity of the situation, the depth of the wrong done, and the potential for a protracted legal battle. Ultimately, however, he chose a different path.

โ€œAfter receiving wise counsel from respected figures in our community and engaging directly with Honorable Chihana, I have decided to withdraw the case,โ€ stated Honourable Chisale. โ€œWhile the severity of the actions deserved prosecution, I have prioritized peace, stability, and the progress of Kasungu Central.โ€

This powerful gesture underscores a crucial understanding: development and progress thrive in an environment of peace and stability. Honourable Chisaleโ€™s actions demonstrate a commitment to putting the needs of his constituents above personal grievances.

This act of reconciliation sets a powerful precedent for other leaders, highlighting the importance of dialogue, forgiveness, and a shared vision for a better future.

The people of Kasungu Central can now look forward to a period of renewed focus on crucial development initiatives, knowing their leader has chosen unity and progress over division. This is a bold and commendable move.

Renowned lawyer Khumbo Bonzoe Soko  writes:Investigators must not play to the gallery, they must play to the Judge. He o...
17/12/2025

Renowned lawyer Khumbo Bonzoe Soko writes:

Investigators must not play to the gallery, they must play to the Judge. He or she is the only one who matters. They must aim to compile a solid docket which closes obvious gaps that defence counsel exploit. In fact, they must work in silence. In the dark literally. Their vindication comes in court.

Otherwise, courts don't traffic in emotions. If an investigation is bungled, cases get dismissed.

It is that simple.

Let's show more sophistication than this.

Address

London

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Low Profile Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Low Profile Malawi:

Share

Category