Katomfu media

Katomfu media 🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Creative studio bringing you innovative storytelling, News, music, sports and lifestyle content from Africa and beyond.
(4)

WhatsApp: Message Katomfu media on WhatsApp. https://wa.me/message/CIWM2UGFUT2JL1 Creative studio bringing you innovative storytelling, music, sports and lifestyle content from Africa and beyond. www.youtube.com/
[email protected]

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩
27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩

1 like. "Brief romantic moments between the characters in Royal Dilemma."

27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Chonde Tamia Jamizo asaone amupweteka mwanayu😉

27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Filimu ya Royal Dilemma yationetsa zinthu🙌.

Adha awawa afila tisanamizane boys🤣

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Coach wa Mighty Wanderers wabwera kuchokera kunja komwe amakaonjezera nzeru za ntchito yake, ndipo zikuoneka k...
27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Coach wa Mighty Wanderers wabwera kuchokera kunja komwe amakaonjezera nzeru za ntchito yake, ndipo zikuoneka kuti anawasowa akazi ake✅

I miss you Babe❣️😊

27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Makolo anu adakusiyirani malangizo ngati Chuma. Dzukani kalimbikireni ✅

27/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Wangodzuka kufikila kuyatsa Data, M'malo moti uchite check ngati ukuyankhula. GOOD MORNING 🌄

26/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩FT: Masters Security 1-0 Chitipa United

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Peter Fote✅
26/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Peter Fote✅

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Banki ya FDH yayima kaye kuthandiza masewero mdziko muno kutsatira kulimbana komwe kulipo pakati pa FAM ndi SU...
26/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Banki ya FDH yayima kaye kuthandiza masewero mdziko muno kutsatira kulimbana komwe kulipo pakati pa FAM ndi SULOM ku nkhani ya mabwalo osewelera mpira.

Masabata apitawo FAM idalamula kuti bwalo la Kamuzu Stadium sililibwino ndipo silinakhoze mayeso oti lidzichititsa masewero m'malo mwake adalitseka.

Koma SULOM sinasinthe masewero omwe idayika kuti Wanderers ikakumane ndi Karonga United pamasewero otsekulira ligi kupatula kuti FAM idawaletsa kutero.

Dzulo laliwisiri Matimu, akuluakulu oyendetsa mpira komanso masapota anakhamukira pa Kamuzu ndipo anali odabwa akuuzidwa kuti masewero alephereka kaamba koti oyimbira sanabwere.

Izi zakwiyitsa Sponsor ndipo wazituluka kaye ponena kuti zikuyipitsa mbiri komanso dzina la kampani yawo. Iwo ati abweranso akakambirana za mgwirizano wawo.

Unduna wa zamasewero unalowelerapo kuti FAM ilore kuti Kamuzu Stadium ingogwirako ntchito pa tsiku lotsekulira lokhalo koma izi siznaphure kanthu.

Yankhulani za kukhosi m'makomentimo✅

25/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Atero

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Timu ya Tottenham Hotspur yapambana koyamba chiloweleni chaka chino cha 2026.Timuyi ikumenya nkhondo kuti isat...
25/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Timu ya Tottenham Hotspur yapambana koyamba chiloweleni chaka chino cha 2026.

Timuyi ikumenya nkhondo kuti isatuluke mu ligi yayikuli yakumangalande ya EPL.

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩 ✅MaBanker ndi omwe akutsogolera table ya FDH Bank Premiership . ✅Silver ndiyokhayo yomwe  yapambana pa match ...
25/04/2026

🔴 #𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩 ✅MaBanker ndi omwe akutsogolera table ya FDH Bank Premiership .
✅Silver ndiyokhayo yomwe yapambana pa match day 1
✅Kamuzu Barracks ndiyomwe yagonja pa match day 1
✅ Bullets, Dedza Dynamos, Civo ndi Moyale Barracks ayamba ndi ma draw
✅Masewero a Wanderers komanso Karonga United alephereka kaamba koti oyimbira sanabwere.
✅Nduna ya zamasewero yawotcha transport itabwelera kwawo osadyetsa maso pa Kamuzu Stadium

Ligi yayamba bwanji? 👇

Address

Chongwe
Lusaka

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Katomfu media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share