Bonkey Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bonkey, brown Street upington, Upington Outlying.
(5)

🌠 Bonkey | Comedy Content Creator
🎬 Creating funny and entertaining videos
🌍 Making the world laugh😂
👉 Follow for daily comedy😁
💫💦 follow me on TIKTOK also👇
tiktok.com/

mayi anga akuti moni nonse pamuzi pano😄🙏makolo sitibitsaa😅😅
22/05/2026

mayi anga akuti moni nonse pamuzi pano😄🙏

makolo sitibitsaa😅😅

21/05/2026

*Ziweto ndi kulira kwake
🐕 Huuuu
🐿️ Myawuuu
🙍‍♀️ Gaire pin 🤣

21/05/2026

"Kukonda munthu olakwika sikut ndi vuto ai"koma kukakamila munthu ot sakukukondani ndye utchisiluwo umenewo😄
gud mornng☺️

akuti wazipha pazifukwa zina zomwe anasemphana ndi bwez lake😪😪abale ife tikusaka akaz ngati awa mpamene akuzipha girls w...
20/05/2026

akuti wazipha pazifukwa zina zomwe anasemphana ndi bwez lake😪😪abale ife tikusaka akaz ngati awa mpamene akuzipha girls why😭

20/05/2026

Girlfriend azikhalako wa kachibwana pang'ono,, timisalaso osati girlfriend maturity phwiii akati akulangize ngati wazaumoyo😂

19/05/2026

Ndende yaikulu kwambiri padziko lapansi ndi banja lomwe mulibe mtendere eeh inu😆😆🙏ka peace of mind kaja mkofunikila🙌

19/05/2026

eeeh koma momwe akundikanila akaziwa or zoti ndizakwatila ndikukayika🤔😭

19/05/2026

ndikadya milomo ndekuti ndiya nsomba 👄kiss kaya nawulawa chaka chiti🙌😭😭

19/05/2026

Tikamakuuzani kuti kubanja mukuondako💔 nde muzinyinyilika🤣

koma mwazuka bwanji?😂

18/05/2026

Ndalama yomweyo akuyidelera girlfriend wakoyo Kuti upatse mayi ako mpaka akuthokoza komanso kukuikizaso mmapemphero🤔😄🙏

kodi akaz inu muti chani kodi 🤣🤣musatengeletu za ine ohooo 😂inetu ngwamisala nkale🤣🤣🤣🙌
18/05/2026

kodi akaz inu muti chani kodi 🤣🤣
musatengeletu za ine ohooo 😂inetu ngwamisala nkale🤣🤣🤣🙌

Address

Brown Street Upington
Upington Outlying
801

Telephone

+265991529051

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bonkey posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Upington Outlying?

Share