DAUDI MTUWA POET

  • Home
  • DAUDI MTUWA POET

DAUDI MTUWA POET Poetry

Bwalo lalikulu loweruza milandu  mawa pa 25 November 2025 likuyembekezeka  kumva ngati kuli nkoyenera kupereka chiletso ...
24/11/2025

Bwalo lalikulu loweruza milandu mawa pa 25 November 2025 likuyembekezeka kumva ngati kuli nkoyenera kupereka chiletso choletsa mzikiti wa Kachanga ku chileka m'boma la Blantyre kupanga adhan.

Sukulu ya Kalibu academy ndi yomwe inapempha chiletsocho ponena kuti kuyitanira anthu ku mapempheroko kukumadzetsa mphokoso lomwe likumasokoneza ntchito ya maphunziro pa sukulupo.

Oweruza milandu Justice Tembo ndi yemwe amvelere mlanduwu.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DAUDI MTUWA POET posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to DAUDI MTUWA POET:

  • Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment?

Share