08/02/2021
INLOVE WITH A GHOST πππππππππππππ
Part 8
INLOVE WITH A GHOST πππππππππππππ
Part 8
Written by Fortune and π king the director sponsored by π BOOK OF STORIES MEMBERS
```
OSAIWALA KUPANGA LIKE BUKU LANGA FACEBOOK PAGE OR KULOWA NAWO GROUP LAULELE THE BOOKπ OF STORIES
```
Mu part yangothai tinalekeza pomwe King ndi Lita amakambirana kuti anvesana kukoma koma ali mkati mokambirana makolo a King anatulukira
''Eish mbola ndi makolo angatu pamenepa nde tipange bwanji ,ndaganiz plan ungo ......
Tipitilize βοΈβοΈ
Ndaganiza plan ungobisala kaye komkuno ndiona kuti ndikutulusa bwanji ,King anapit kukatsekula kuti makolo ake alowe
''Kuchita kuzitsekera chonchi bwanji komaso ndanva mau a munthu mnyumba muno talandira alendo kapena anafikira kulalamuka mai ake
''Mmmmm......uje.....kungot......ujeni amai ndimayankhura foni inuyo simunanve bwino komaso sitinalandire mulendo aliyese kuno ,kulikulunga bodza king
''Ukunama iwe ndanva mau a mkazi muno odi ndipite kuchipinda kwako komweko usandipusise ndine wamkulu
Mai a King anapita kuchipinda komweko kukasaka anayang'ana palipose koma sanapezeko munthu momwe zimachitika zonsezi bambo a King ali poteropo kumangoonerera poti nawoso pena samatha kuwanvesa akazi awo muzochitika
''Wapulumuka nkanangopezako munthu ukanandiziwa lero
King chongonva mau ameneyo mtima wake unatsikano sanalankhuleso koma kulunjika kuchipinda kwake komwe anayamba kumusaka bwenzi lake koma zinali zodabwisa sanapezeko aliyese ''eish wapitaso kuti mkazi uja kungosowa basi π€π€π€π€ndikuyenera kuchitapo kanthu
King anakhala kulingalira kuti pamenepa apange bwanji ali mkati molingalira anagona chi turo ,kumbali ya Lita atatsala ku chipinda kuja anali ndi mantha komaso amaganiza kuti atuluka bwanji mnyumba ya eni kenako nnangoona pomwe anakhalapo wasowapo nane sindikudziwa kuti anapanga bwanji
King atadzuka anaganiza zomuyendera mzake Manze poti panali patatenga nthawi asanaonane komaso akamufotokozere zomwe zachitika kwawo ,King anayenda changu ndipo anayenda ka nthaw kochepa anali atafika komwe anamupeza mzakeyu akuchapa
''Man King sopano lero mwaganiza zotiyendera after kusowa kapena mula akukupasani ma busy et uyutu anali Manze kumulandira mzakeyu
''Eish man ndabalalika moti kubweraku nkhani yake ndi yomweyo ya alamu anuwo
''Inutu akazi akuphani kkkkkk chifukwa nde zikuoneseratu kuti suli bwino nde tanenani chachitika nchani
Apatu king anamufotokozera mzakeyu momwe zinakhalira ndipo naye anali asakunvesa ndipo anafusa avekere
''Nde mwati kungosowa basi ,koma mkazi ameneyu akundidabwisa koyamba unandiuza kuti nthawi zonse amaimba ndiyeyo iwe kuti uimbe foni simapezeka lero ndi izi zongosowazi nsaname ndili ndi mantha bola ungomusiya upeze wina
''Hey! Manze ngat zili zomusiyazo nde uiwale mkazi amene uja momwe ndimamukondera nde iwe uziti ndimusiye ndimaona ngati undiuza za mzeru
''Ine palibe cha mzeru chomwe ndikuona koposa kuti ungomusiya mkaziyo ,kapena ufuna uzanve nkhwanga ili mmutu eti
Anyamatawa atamaliza macheza awo King anatsanzika kuti akupita ndipo Manze anamuperekeza koma King maganizo onse anali kwa bwenzi lake iye mfundo yoti amusiye samagwirizana nayo
''Eish zoona ndimusiye Lita koma ine mkazi uja ndimamukonda kwambiri ndipo sindingapange mistake iliyose nzalolera kuyambana ndi aliyese ofuna kutisokoneza odi ndingomuimbira ndimufuse kuti dzuro lija anachokako bwanji kunyumba ,King anayesera kuimba kangapo koma zachisoni foni simapezeka
King ali mkati molingalira foni yake inayamba kuitana atapanga check anapeza kuti inali nambala ya chilendo
''Hello ndikuyankhula ndi ndani ine ndi King
He.......tu...tu...tu .......
Tikumane mu part yotsatirayo
Mu part yangothai tinalekeza pomwe King ndi Lita amakambirana kuti anvesana kukoma koma ali mkati mokambirana makolo a King anatulukira
''Eish mbola ndi makolo angatu pamenepa nde tipange bwanji ,ndaganiz plan ungo ......
Tipitilize βοΈβοΈ
Ndaganiza plan ungobisala kaye komkuno ndiona kuti ndikutulusa bwanji ,King anapita kukatsekula kuti makolo ake alowe
''Kuchita kuzitsekera chonchi bwanji komaso ndanva mau a munthu mnyumba muno talandira alendo kapena...? Anafikira kulalamuka mai ake
''Mmmmm......uje.....kungot......ujeni amai ndimayankhura foni inuyo simunanve bwino komaso sitinalandire mulendo aliyese kuno " analikulunga bodza king
''Ukunama iwe ndanva mau a mkazi muno odi ndipite kuchipinda kwako komweko usandipusise ndine wamkulu
Mai a King anapita kuchipinda komweko kukasaka anayang'ana palipose koma sanapezeko munthu momwe zimachitika zonsezi bambo a King ali poteropo kumangoonerera poti nawoso pena samatha kuwanvesa akazi awo muzochitika
''Wapulumuka nkanangopezako munthu ukanandiziwa lero
King chongonva mau ameneyo mtima wake unatsikano sanalankhuleso koma kulunjika kuchipinda kwake komwe anayamba kumusaka bwenzi lake koma zinali zodabwisa sanapezeko aliyese ''eish wapitaso kuti mkazi uja kungosowa basi π€π€π€π€ndikuyenera kuchitapo kanthu
King anakhala kulingalira kuti pamenepa apange bwanji ali mkati molingalira anagona chi turo
"...Lita atatsala ku chipinda kuja anali ndi mantha komaso amaganiza kuti atuluka bwanji mnyumba ya eni kenako anayamba kuseka mokuwa ndimosokosela koma chodabwisa palibe olo ndi modzi yemwe anamva kukuwaku
".. Lita mwakamphindi anapenzeka akuyenda chapabwaro pa nyumba ya makolo a King
Bambo a King adangozizimuka akuona chiphadzuwa koma nkuti anali akumalizika kuonesa mbuyo... Anaonadi ndi maso awo koma osakhulupilira chifuka amaoneka owala ndi zovala zonyezimila ngati ngero weni weni komanso china chomwe sadaganizileko ndichoti maonekedwe ake anali oti umphawi wa mwana wao sangagwile ka ngenge ngati kameneka ndipo maganizo awo adangokhala oti basi mwina mlendoyu anasokera
King atadzuka anaganiza zomuyendera mzake Manzy poti panali patatenga nthawi asanaonane komaso akamufotokozere zomwe zachitika kwawo ,King anayenda changu ndipo anayenda ka nthawi kochepa anali atafika komwe anamupeza mzakeyu akuchapa
''Man King sopano lero mwaganiza zotiyendera after kusowa kapena mula akukupasani ma busy et uyutu anali Manzy kumulandira mzakeyu
''Eish man ndabalalika moti kubweraku nkhani yake ndi yomweyo ya alamu anuwo
''Inutu akazi akuphani kkkkkk chifukwa nde zikuoneseratu kuti suli bwino nde tanenani chachitika nchani ...?
β, , , Apatu king anamufotokozera mzakeyu momwe zinakhalira ndipo naye anali asakunvesa ndipo anafusa avekere
''Nde mwati kungosowa basi ,koma mkazi ameneyu akundidabwisa koyamba unandiuza kuti nthawi zonse amaimba ndiiyeyo iwe kuti uimbe foni simapezeka lero ndi izi zongosowazi nsaname ndili ndi mantha bola ungomusiya upeze wina
''Hey! Manzy ngat zili zomusiyazo nde uiwale mkazi amene uja momwe ndimamukondera nde iwe uziti ndimusiye ndimaona ngati undiuza za mzeru
''Ine palibe cha mzeru chomwe ndikuona koposa kuti ungomusiya mkaziyo ,kapena ufuna uzanve nkhwanga ili mmutu eti, , , , ?
Anyamatawa atamaliza macheza awo King anatsanzika kuti akupita ndipo Manzy anamuperekeza koma King maganizo onse anali kwa bwenzi lake iye mfundo yoti amusiye samagwirizana nayo
''Eish zoona ndimusiye Lita koma ine mkazi uja ndimamukonda kwambiri ndipo sindingapange mistake iliyose nzalolera kuyambana ndi aliyese ofuna kutisokoneza odi ndingomuimbira ndimufuse kuti dzuro lija anachokako bwanji kunyumba
Kingπ anayesera kuimba kangapo koma zachisoni foni simapezeka
King ali mkati molingalira foni yake inayamba kuitana atapanga check anapeza kuti inali nambala ya chilendo
'' Hello ndiine king koma ndikuyankhula ndi ndani...?
"...He.......tu...tu...tu .......π΅
WAIT FOR NEXT PART
Madzi ayamba kuchita katondo zosasimikizika kuti Lita ndi ndani Ku mtundu wathu chonde ndikufuna zimacomment kuti nkhani imveke bwino
Tikumane mu part yotsatirayo...By Fortune ender π king chidzukulu the director and sponsored by πBOOK OF STORIES WHATSAPP GROUP
Ladies and gentlemen i cares of you guys but what i need from you is encourage and support for my story writing and funny videos
you are welcome feel at home