Thoxy Wiliford

βœ… Mulungu asinthe misozi yanu kukhara umboni ndi nkhondo zanu zikhala chipambano mu m'dzina la lamphamvu la Yesu khrisit...
04/10/2026

βœ… Mulungu asinthe misozi yanu kukhara umboni ndi nkhondo zanu zikhala chipambano mu m'dzina la lamphamvu la Yesu khrisitu Amen πŸ™πŸ™πŸ’š

βœ… Nthawi zina mulungu amagwilitsa ntchito kukanidwa ndi kusalidwa kwathu potipulumutsa kwa anthu omwe anali ndi zolinga ...
04/10/2026

βœ… Nthawi zina mulungu amagwilitsa ntchito kukanidwa ndi kusalidwa kwathu potipulumutsa kwa anthu omwe anali ndi zolinga zoipa pa ife πŸ™πŸ™πŸ’š

βœ… Pamene ukulimbikira k*ti nyengo zako  zisinthe ena ali busy kusaka njira zokugwetsera,Mulungu awachititse manyazi. Ame...
04/10/2026

βœ… Pamene ukulimbikira k*ti nyengo zako zisinthe ena ali busy kusaka njira zokugwetsera,
Mulungu awachititse manyazi. Amen πŸ™πŸ™πŸ’š

βœ… Take 2 second to say thank you God
03/10/2026

βœ… Take 2 second to say thank you God

βœ… Azibambo kuseliku azimay abweza moto ak*t iwo sik*t samafuna kulera a bambo owapezamo ayi km vuto lalikulu ndife aziba...
03/10/2026

βœ… Azibambo kuseliku azimay abweza moto ak*t iwo sik*t samafuna kulera a bambo owapezamo ayi km vuto lalikulu ndife azibambo omwe sitifuna kufotokoza zithu bwn pachiyambi, ndy zimapezeka kt mkaz tankhara nawo 5 years osafotokozera chilichonse mwamwayi mulungu wadalitsa banja zithu zayamba kuyenda ndipomwe timabwera kulula zoona zake ndy iwo atemetsa nkhwanga pamwara k*t sagaloleπŸ˜‚

Komas ak*t Azibambo ife ndi oyipa kuwapoosa azimay maka tikakwatira mkaz oti ali ndi ana kale tomawachitira nkhanza ana ndi zija zimapezeka kt zibambo ukupita kuntchito wandinda chida mutanga waufa πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚ kumawadya ana zimalabara anakhara wakaz kumamuthira batirey

Azibambo a zanga mwankhara pat zikamba azimayi zoona kapena agotinamiziraπŸ˜‚πŸ˜‚ tiyen mu comment section tikachezaπŸ‘‡πŸ‘‡

βœ… Chinthu chopwetekesa mtima ndikulephela k*thandiza banja lako chifukwa ndiwe osaukaπŸ˜₯ Ambuye mkumbukileni mwana wanuπŸ™πŸ™ ...
03/10/2026

βœ… Chinthu chopwetekesa mtima ndikulephela k*thandiza banja lako chifukwa ndiwe osaukaπŸ˜₯ Ambuye mkumbukileni mwana wanuπŸ™πŸ™
😭😭😭

βœ… Azanthu ena sanakwanitse udzuka ndi moyo koma ife mwatikondera. Ambuye tathokozaπŸ™πŸ™πŸ’š Amen
03/10/2026

βœ… Azanthu ena sanakwanitse udzuka ndi moyo koma ife mwatikondera. Ambuye tathokozaπŸ™πŸ™πŸ’š Amen

βœ… Mau a mulungu ndiwo nyali ya moyo wanga. Amen πŸ™πŸ™πŸ’š
02/10/2026

βœ… Mau a mulungu ndiwo nyali ya moyo wanga. Amen πŸ™πŸ™πŸ’š

βœ… Mulungu akumbukile iwe, ukuwerengawe ndi banja lako. Akuchotsele, chitozo apange misonzi yako kukhala ya chimwemwe. Am...
02/10/2026

βœ… Mulungu akumbukile iwe, ukuwerengawe ndi banja lako. Akuchotsele, chitozo apange misonzi yako kukhala ya chimwemwe. Amen πŸ™πŸ™πŸ™πŸ’š

Address

20372
Kimberley
8301

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Thoxy Wiliford posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category