Sele Melodies CCAP choir.

  • Home
  • Sele Melodies CCAP choir.

Sele Melodies CCAP choir. This is a Gospel choir from Salima under CCAP Nkhoma Synod, Mpatsa CCAP Mission, Sele Prayer House

At amaliza maeso aja😅koma mukhoza inu?
11/06/2026

At amaliza maeso aja😅

koma mukhoza inu?

Tili ndi ana pafupifupi 6 akulemba maeso, all the best.🌟
08/06/2026

Tili ndi ana pafupifupi 6 akulemba maeso, all the best.🌟

03/06/2026

Taluza nsanamila ina Mr Ngolomi iiiii mau tilibe

26/05/2026

Colona virus uku😅

Osamathamangila zinthu zoti nthawi yake sinakwane Mulungu sakondwera Congratulations Arsenal after 22 years
20/05/2026

Osamathamangila zinthu zoti nthawi yake sinakwane Mulungu sakondwera
Congratulations Arsenal after 22 years

18/05/2026

Lero takwanisa za 7

17/05/2026

Tikuitanani tsiku lina tizacheze😁

14/05/2026

Ngati munavera album yathu yonse iyi mutu wake ndi chani?

12/05/2026

Pano tufuna tiyambe campaign anyamata a Bass(Besi) akwatire chifukwa sizoona ai😅

Lero tati tibwerereko mbuyoMwadziwapo ndani apa😅
07/05/2026

Lero tati tibwerereko mbuyo

Mwadziwapo ndani apa😅

Address

Salima

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sele Melodies CCAP choir. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Sele Melodies CCAP choir.:

  • Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment?

Share