07/11/2022
Wamzeru ndan apa?**
nd zaya #
Bengo anapta kumunda kukayendera mbeu zake, atafka adamva phokoso mbal ina yamunda wake, apa Bengo adayenda monyang'ama kupta k*t akaone chkuchtka , atayandkra adaona munthu wina akudula nthochi zake apa Bengo adatulukra ndkugwra okubayo apa Bengo sadafuule adangomutenga nkumapta naye kufolamu., Alnkat mwasewu okuba uja adayakhula mozchepesa kmaso modandaula, abwana ndmat mundlole ndbwelere ndaywala thumba lozaza nd nthochi ndnasunga mmalile muja cholnga umbon kufolamu uzkakwanra , apa Bengo atamva amvekere mbamva yamzeru, ine ndkhala p***a kukudkra koma changu wamva!
Mbamva ija itabwelera snabwelereso apa k*t Bengo akudklra atalema kudkra ananyamuka nkumapta kwanzake zaya, anayankhulana motere
Bengo; Zaya! Zaya! Zaya! Ooooooo..... Ku..... baaaqq
Zaya; aaaa, aaaaaaalik*ti?
Bengo; ndne wa mway ndnagwra wakuba kumunda kwanga,
Zaya; ndwe wamway ? Okubayo alpat kod ndk*t alik*t!!
Bengo; zaya,! Dekhan , iwe mphuma bwanj umafuna umuotche kod? Okubayo ndwako kod?
Zaya; chabwino znakhala bwanji?
Bengo; ndnagwra okuba nde amat waywala thumba lomwe anabsa nde anapta ine mkumamudkra k*t ukakhale umbon ku folamu nde pompo sanabwelere,
Zaya; aaaa ndwe opusa, apa zaya adamenya Bengo mbama,
Bengo; sopano bwanj?
Zaya; ndkanakhala ine sndkanatero , ndkanapta ndekha kumundako, iye nkumusya pamseu pomwepo k*t ndkamabwera ndmupeze pomwepo.
Continue...........
Just comment to proceed