Mlakatuli Weston Phamba

Mlakatuli Weston Phamba "Iwo amatero, Inu mukutinji?" Poet Aspiring writer

YouTube Channel: https://youtube.com/?si=t-10Dg1KNAwImuCV

Mwina nkutheka mumakhala ku Zomba kapena ayi mawali, lachisanu pa 10 April mupezeka mu Zomba. Tadzagaweni nthawi yanu pa...
09/04/2026

Mwina nkutheka mumakhala ku Zomba kapena ayi mawali, lachisanu pa 10 April mupezeka mu Zomba.

Tadzagaweni nthawi yanu pang'ono pokha mukasangalale ndi ndakatulo komanso zochitika zosiyanasiyana pamene Biko Mlakatuli akupanga launch chimbale chake choyamba cha ndakatulo chotchedwa .

Malo: Room A, University of Malawi

Nthawi: 6 kololo madzulo

Tikakumane komweko 🔥🔥🔥

26/03/2026

Kuwazepula mayina a eni ake mu ndakatulo kuti zepu zepu ��

New poem on the World Poetry Day and Eid Mubarak Day Link ili mu comment section. Happy World Poetry Day to all poets an...
21/03/2026

New poem on the World Poetry Day and Eid Mubarak Day

Link ili mu comment section.

Happy World Poetry Day to all poets and poetry lovers and Happy Eid Mubarak to all Muslim friends.

31/12/2025

Chaka chikutha bwanji mbali imeneyo?

Kuno ndiye chikutha bwino zedi.

Ndi chaka chomwe chandipatsa ndakatulo zokwana zisanu ndi imodzi zomwe ndi:

1. Chipondamthengo
2. Ndiwe mthakati?
3. Mubwere ku Ukachenjede
4. Kadzidzi
5. Usi Masamba - Ubwera Liti? ft Weston Phamba
6. Unima Class of 2026 - Mundimvetsetse Munthune

Inu munakondwa nayo kumvera ndi iti ?

Ena nkutheka sinamvereke ndakatulozi ndiponya ma link omwe mungapezere ndakatulozi kuti inunso mumve kukoma pamene tikukwangula chakachi.

Ulemu ndi matamando zipite Kwa Mulungu mwini wake chifukwa cha luso ili komanso ndithokoze inu nonse amene mumakhala pamenepo nthawi Zonse kupanga support luso langa mu njira zosiyanasiyana.Pitirizani kutero chifukwa ndakatulozo ndiye zikadabwera.

19/11/2025

Ndakatulo

ya

"KADZIDZI"

mu comment section.

15/10/2025

Kwatuluka kanema wa ndakatulo yanga ya tsopano. Ndi mphatso yopita Kwa anakubala onse.

Link yake ilimo mu comment section tikaonere limodzi ku YouTube ko!!!

11/10/2025

Kuchokera ku Ulumba Poetry Group kwatuluka ndakatulo ya tsopano madzulo omwe ano.

Tiyeni tikamvere tonse ku YouTube ko. Link mu comment section 🔥

Ndinangoiwala kulengeza  koma mphatso za birthday zafika ndithu. TNM (Telekom Networks Malawi) komanso Florence Lucy Msu...
25/09/2025

Ndinangoiwala kulengeza koma mphatso za birthday zafika ndithu.

TNM (Telekom Networks Malawi) komanso Florence Lucy Msukwa birthday talandira 🥳🥳🥳

05/09/2025

Tinali limodzi dzulo ku Writers Workshop ku University of Malawi, tadyera ndakatulo limodzi
Kusinthana stage imodzi
Osadziwa lero ndi birthday yake

Happy birthday Mlakatuli Brighton Alfred

Chaka chokoma ndi kulemba ndakatulo zothyakuka.

It's an honor. And personally, I am encouraged and thankful 🙏
05/09/2025

It's an honor. And personally, I am encouraged and thankful 🙏

UNIMA FINALES TURN THEIR JOURNEY INTO POETRY

Final-year students at the University of Malawi have come together to present a poetry medley titled “Mundimvetsetse Munthune”, crafted to reflect their academic journey from first year to final year.

The piece blends Chichewa, Chitumbuka, and English to express the challenges they faced, the lessons they learned, and the dreams they continue to carry.

The title “Mundimvetsetse Munthune”, meaning “You ought to understand me”, was chosen to speak to the depth of their experience and invite others to connect with their story.

Florence Msukwa, Annie Mushe, Duncain Matupi, Godfrey Fossah, Austin Kafanikhale, Steve Gwiriza, and Weston Phamba performed the medley to honour their shared journey and give voice to the emotions behind their success.

Lead coordinator Weston Phamba told Chanco News that the medley is created to speak for every student who has walked this path.

And one of performers Steve Gwiriza added that it is not just a poem but a heartbeat, meant to express what words alone could not.

The medley will be premiered tomorrow during the Finale Victory Dance.

In the picture: Weston Phamba.

Reported by Kenneth Zindondo.

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mlakatuli Weston Phamba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Mlakatuli Weston Phamba:

Share

Category