16/02/2025
MISSING PERSON ALERTβΌοΈ
MUNTHU WASOWA
Dzina lake Hamidah Saidi
Anaoneka kosiliza pa ITG Mu Limbe pa nthawiyi anavala malaya a black ndi chitenge amaphunzila ku madalitso High School kwa Manje(Blantyre)
Ngati mungamuone imbani ma nambala awa
0884426408
0996795960
0886339532