Bvumbwe Tv

Bvumbwe Tv Good Time For Good People

Happy BirthdayNyamata wa Kwa bvumbwe wa Luso La zolembalembaKomanso Kupenta ManyumbaMonga mwa nthawi Zonse..... Langinza...
19/08/2026

Happy Birthday
Nyamata wa Kwa bvumbwe wa Luso La zolembalemba
Komanso Kupenta Manyumba

Monga mwa nthawi Zonse..... Langinzani Munthu anthu a mulungu,

Dzina Lake ndi Pemphero Chiwaya (C pex Arts) Ndipo Shop yake Ili PA ligowe, PA ntunda pake po.... Ambiri amangoti PA a Mbewe,๐Ÿค”โšก

Bvumbwe Tv

Anthu akufuna kwabwino Akupitiliza kupanga Donate ZinthuZothandizira Maphunziro Komanso Umoyo wa Ana Omwe Ali manja Mwa ...
19/08/2026

Anthu akufuna kwabwino Akupitiliza kupanga Donate Zinthu
Zothandizira Maphunziro Komanso Umoyo wa Ana Omwe Ali manja Mwa Bungwe La
Destiny Kids Foundations
Kuchokela kwa Khumbanyiwa

Ndipo Munthu wina yemwe Sanafune kuti Timutchule Dzina, Wapeleka Zovala Kuti Anawa akagawilidwe,๐Ÿ‘Œโšก

Tisaiwale kuti Cholinga Cha Bungweli ndi kupatsa ana mwayi wophunzira komanso kukhala ndi tsogolo Labwino, posatengela m'mene Mabanja awo aliri

Tonse Tingathe โšก๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ
Bvumbwe Tv

18/08/2026

Zukhala bwanji Kodi??
Eeeehhhhh๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿค”

18/08/2026

Chaka chino Ambiri
Kwa bvumbwe kuno Akukwatiwa

Amen mpingo ๐Ÿ™๐Ÿ™

Potengelaa report Ena komanso Vn yomwe Yatipeza ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œโšกโšก๐Ÿค”Pa Nkhani yokhunza Maliro a mwana yemwe wafela ku thezoMwana yemwe ...
18/08/2026

Potengelaa report Ena komanso Vn yomwe Yatipeza ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œโšกโšก๐Ÿค”
Pa Nkhani yokhunza Maliro a mwana yemwe wafela ku thezo

Mwana yemwe watisiyayi, Anali Akutumidwa ndi mai wina
Wa ku ntundu, Mu njira ya ufiti ndithu(Masenga)..
Ndipo zakhala zikuchitika kwa kanthawi, Mpaka Angaliba Anakadandaula ku ntundu kwa mwanayi, Za momwe Mwanai ndi Mayi wina wa ku khomo amachitila Zinthu zawo kunja kukada๐Ÿ‘Œ

Ndipo ku madzi ko, Kunasowa Makhwala komanso Dzira Lomwe Linali mu SUPA, mwanayi Analimwa

Nde chongomwa Dzira lo, komanso Kusowesa Makhwala, Mwanai anayamba Kusowa mphavu, Ndipo Akuti Chinachake chimangomukwapula ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ.. Mpaka anakwanisa kuulura Za momwe wakhala Akuchitila Zamasengazi, Limodzi Ndi mayi omwe amamutumawo

Angaliba wo, chomwe Amafuna ndi choti Katundu wawo abwele,
Ndipo Otuma mwanai, katundu sanabweze eeeeehhhh,

Nde Makhwala yake ija, Basitu Mpaka mwana wapita nawo.๐Ÿค”๐Ÿค”๐Ÿค”
Akulu Akulu, Zotambisa anazi si zabwino

17/08/2026

Mpaka A police Aotcha Simba

mukhale Pompo ๐Ÿšจ๐Ÿ‘ฎ๐Ÿ™Œ

17/08/2026

Escom iweo๐Ÿค”๐Ÿค”

Ayiii zikomo ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ

Kuno kwacha bwinoKaya kumeneko????Bvumbwe Tv
17/08/2026

Kuno kwacha bwino
Kaya kumeneko????

Bvumbwe Tv

Kuzera mu mphekesela Zomwe zikumveka ,Ntchito Yomanga Filling station pa malo pomwe Pamaziwika ndi dzina Loti Pa Belerin...
16/08/2026

Kuzera mu mphekesela Zomwe zikumveka ,

Ntchito Yomanga Filling station pa malo pomwe Pamaziwika ndi dzina Loti Pa Belerin ,yayambika,ndipo Ngalande za Malire Zaikidwa ndithu๐Ÿคทโ€โ™‚๏ธ......

Koma anzathu a Kachisi wa,Ofunika Kuwanganizila ka malo kosewelera ana ...

Bvumbwe Tv
Sunday Masana

From ImboxHey Admin, Tatola Chiphaso Cha UnzikaKu Nsika kwa Bvumbwe, Nde Mwina alipo angawazindikire Ayiniake a chinthuc...
14/08/2026

From Imbox

Hey Admin, Tatola Chiphaso Cha Unzika
Ku Nsika kwa Bvumbwe, Nde Mwina alipo angawazindikire Ayiniake a chinthuchi ๐Ÿ™Œโšก

Kwa omwe tilinawo pafupi, Tifikisileni uthenga wu
Kuti azatenge Katundu waoyi... Osaiwala, chiphaso cha unzinka ndi chofunika kwambiri

Bvumbwe Tv
0882619985

Address

Bvumbwe Trading Centre
Thyolo

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bvumbwe Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share