POET SISCO

POET SISCO poem writter

28/06/2026

Mon
upite kwa wina aliyese
pamudzi pano

21/06/2026

Kutumikira Mulungu

Tiyeni ku YouTube
16/05/2026

Tiyeni ku YouTube

" This poem pays homage to the musicians who left us too soon. With words that echo the sorrow of their passing, it captures the essence of their art and the...

22/04/2026

TOP FUN OF BLACK MISSIONARY

Muzindiwelengera gulu la anthu ONENEPA 🫣osaiwala any day timvera ndakatulo kuchokera mwa DUNTU SISCO ,ondikonda amanditc...
20/04/2026

Muzindiwelengera gulu la anthu ONENEPA 🫣

osaiwala any day timvera ndakatulo kuchokera mwa DUNTU SISCO ,ondikonda amanditchura SISCO WA NJODO

Zikomo kwambiri popeza mudandipatsa lunso ,chifukwa cha lunso lomwe munandipasa ena amakodwera pamene ena sangakondwere ...
17/04/2026

Zikomo kwambiri popeza mudandipatsa lunso ,chifukwa cha lunso lomwe munandipasa ena amakodwera pamene ena sangakondwere popeza palibe munthu amene angasangalase wina aliyese padziko lino lapansi

Nditalengeza kuti za ndakatulo ndazisiya,ndidalandira mafunso ochuluka kwambiri ndipo ena mwa iwo amadandaura ,sopano pano ndabwera kuzapitiliza ntchito yanga yomwe mudandipasa ,ndakatulo zomwe ndikufuna kutulusa ndi monga

(1)KODI ALIKUTI
(2)MTENDERE WAMUMTIMA
(3)KACHITSIRU
(4)UZAMENYESA AKWANU
(6)KWATHU
(7)KAMWINI WAKWALOLO
AMEN

08/04/2026

Ma dance abwino

05/04/2026

Muwuzen Mulungu zosowa zanu

03/01/2026

Morning 🌄

Address

Thyolo

Telephone

+265880066816

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when POET SISCO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category