Ntchisi Ccap Police Nursery Choir

Ntchisi Ccap Police Nursery Choir We Sing To Praise The One Who Gave Us Voices. 🙌🎤

07/06/2026

AMBUYE MUTICHOSERE NTIMA ODZIKUZA
AMEN

22/05/2026

COMING SUNDAY TIPEREKA MPHOTO KWA MA KOMANSO ALIYESE AMENE ANAPANGAPO SHARE MA POST ATHU HAVE A NICE DAY

22/05/2026

TODAY IS FRIDAY INSTEAD OF WAITING FOR BEER JUST THANK GOD TO REACH THIS FAR

21/05/2026

AMBUYE AZAKHALA AKUKUSAMALANI KUFIKIRA MUZAFE JUST CHOOSE KUMUYAMIKA
🙏🙏

12/05/2026

MULUNGU SANGALENGE MUNTHU K*T AZAKHALE MOZUZIKA PA ZIKO LAPASI
JUST WAIT ALINANU NDI CHOLINGA

27/04/2026

olemba uthenga amalemba mwa simple koma owerenga ndiyemwe amapindula ambuye mudalise yense anena AMEN ndi ntima onse AMEN
🙏

HAPPY SUNDAY FAM😊😊TIYEN KU CHURCH
26/04/2026

HAPPY SUNDAY FAM😊😊
TIYEN KU CHURCH

NYIMBO ZATHU ZIKUPEZEKA PA YOU TUBE ���
26/04/2026

NYIMBO ZATHU ZIKUPEZEKA PA YOU TUBE ���

Share your videos with friends, family, and the world

23/04/2026

ZKOMO AMBUYE POTIFIKISA MAZULO ANO TITETEZEN PAMENE TIKUGONA
AMEN...!

21/04/2026

KUGONA NDI CHIZOLOWEZI KOMA KUZUKA NDI MOYO NDI CHISOMO CHA MULUNGU HAVE A BLESSED NIGHT 🙏

Address

P. O. Box 49, Ntchisi
Ntchisi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ntchisi Ccap Police Nursery Choir posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share