Mfana Elisah

Mfana Elisah Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mfana Elisah, Arts and entertainment, kasakula, Ntchisi.

27/03/2026

Anga fiile bwanji machimo, koma azayayeletsa ngati matalala🙏🙏

27/03/2026

Go away
Come again never

22/09/2025

Hello amalawi anzanga! Nthawi yakwana yokhatu apa🤩🤩🤩🤩

14/08/2025

Mayeso atuluka uku🤫🤫🤫🤫thamanga kwone😳😳😳😳😳

06/02/2025

Choyipa chitsata mwini! Tsizinamtole wina m’boma la Mangochi ali muululu pomwe wabayidwa pa mimba ndi wagulu lake lomwe pomwe amafuna kubaya munthu wina yemwe amafuna kumuchita chiwembu.

Patsiku latsokali, Victor Chisuse wa zaka 20 adatengana ndi wa manja lende nzake, ulendo okabilibinya anthu m'misewu. Atangoti gululu ndi James Nansenyaname yemwe amayendera zake, mbavazi zidangoti laponda lamphawi, kuyiwara kuti kandiyelekere adagwera m'mpheto mwapongozi.

Adakadziwa adakaphika therere; Awiriwa adamulanda foni Nansenyaname kuyiwala kuti mamuna nzako mpachulu. Kafa nikhaleyu adayamba kusintha zibonyongo ndi awiriwa. Atazindikira kuti ashosha mavu nkhomola, m’modzi mwa akathyaliwa adakuwa, “tangomubaya basi.”

Imodzi mwa mbavazi yomwe pano siikudziwika komwe ili, idasolora lupanga. Koma poti tsiku la tsoka amakuluma ndi wako yemwe, m’malo mobaya Nansenyaname, kapsalayu adaphonya ndikubaya nzake, Chisuse pamimba. Atazindikira, adaliyatsa la mtondo wadooka kumusiya Chisuse akunong'oneza bondo kwinaku akusamba mwazi.

Nsamaliya wina wa chifundo adatengera mbavayi pamodzi ndi Nansenyaname ku chipatala komwe wachiwembuyu wagonekedwa pomwe Nansenyaname adatulutsidwa nthawi yomweyo

Dinani apa kuti zambiri zisakuphonyeni

09/09/2024

Address

Kasakula
Ntchisi

Telephone

+265990576174

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mfana Elisah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share