Advent Yohane Mogesi

Advent Yohane Mogesi Proclaiming the Advent of Jesus Christ

23/10/2025

Did you know that just alook at sombedy's profile you can know the character of that person.

To whom it may concern,Program yomwe Boma lachita pogula chimanga ija ndiyamikile ngati nzika, koma pempho likhale lokut...
23/10/2025

To whom it may concern,

Program yomwe Boma lachita pogula chimanga ija ndiyamikile ngati nzika, koma pempho likhale lokuti asagawe mwaulere koma achiike ma admarc ndikuika Marengo otsika izi zothandizidwa kuti chimanga pansika chitsike ndunena izi pa experience

1, nthawi ya DPP ndi MCP anthu omwe amapindura kwambili anali achipani osati ovutika, chitsanzo anthu omwe amakhara marent matownship olo atakhara atha zaka zambiri sawalemba amati ndiobwera yet kukachitika maliro amakapempha Ufa mmakomo mwawomo, akuluakulu azipani ndimafumu amalembana matumba oposera limodzi olo Ena amalemba maina awana wawo omweso ndiosaima pawokha pomwe anangondo okalamba sanalembe kapena ngati awalemba ndekuti thumba limodzi agawana anthu 6.

Kugawa chimamga chaulere kumapeleka mabvuto awuphawi chitsanzo a MCP anagawaso chimanga koma sichinatsike mtengo pazifukwa zakuti ambiri anaikapo dyera ndipo opindura anali anthu osayenera chitsanzo ngozi inachitika kublantyre chilimba pa Dennis anthu anakhudzidwa anali olemera kale, komaso anthu amachita nazo ngozi zomwe zimapeleka mbiri yoipa kuboma kuti mmafuna magazi awanthu.

Pomaliza nakakonda kuti chimangachi chiikidwe ma admarc ndichitetezo kuti ogula asakhare mavenda koma osauka.

Kumapeto ndiseke kuti Boma mene likugura chimanga angakhaletu sichinatsike koma andale kpn KT achipani alembanatu kale🤣🤣🤣🤣

Yesani kusintha chitani kusintha

Address

Chilimba
Ndirande

Telephone

+265883884987

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Advent Yohane Mogesi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share