Adake Phule Entertainment

Adake Phule Entertainment Comedian

With Promise Justine – I just got recognised as one of their top fans! 🎉
19/05/2026

With Promise Justine – I just got recognised as one of their top fans! 🎉

Ndili ndi 20pin panopa ndiyipeleke Kwa Munthu mmozi Amene angakwanise kutchula maina a anthu awa onse ndima surname awo
19/05/2026

Ndili ndi 20pin panopa ndiyipeleke Kwa Munthu mmozi Amene angakwanise kutchula maina a anthu awa onse ndima surname awo

15/05/2026

Lazarus Chakwera amuthila tear gas Ku mwambo wa Kamuzu

Ndawondwa kwambiri munthune mkuwona bwaa?
15/05/2026

Ndawondwa kwambiri munthune mkuwona bwaa?

Thank you mabwana ndi Madonna ndalama ndinalonjeza zija ndapeleka ngati simnalandile ikani number yanu mu comment box ku...
13/05/2026

Thank you mabwana ndi Madonna ndalama ndinalonjeza zija ndapeleka ngati simnalandile ikani number yanu mu comment box kuti mawa yisazakuphonyeni

13/05/2026

Pelekani ma number ndikugawa kenakake yikakwana 4:30PM
Akhale a Airtel

13/05/2026

Akwawo Kwa Morton Baghaya awa akuti Chani?

Ndinavala Spanner ya Spanner Chifikileni kunyumba zulo mitanda iwili siyikundikwana ndipange bwanji?
13/05/2026

Ndinavala Spanner ya Spanner
Chifikileni kunyumba zulo mitanda iwili siyikundikwana ndipange bwanji?

Anytime ndigawa mtonyo pangani invite anzanu tikwane 200 Pano zisakuphonyeni msachite kusowa bundle ine ndilipo
13/05/2026

Anytime ndigawa mtonyo pangani invite anzanu tikwane 200 Pano zisakuphonyeni msachite kusowa bundle ine ndilipo

Timapezeka ndi Mbeu ya Mitengo monga M'bawa, Mwavi, Msambafumu, Tsanya, Mthethe, Mgoza etc Za zipaso zokwatisa nazoso zi...
13/05/2026

Timapezeka ndi Mbeu ya Mitengo monga
M'bawa, Mwavi, Msambafumu, Tsanya, Mthethe, Mgoza etc
Za zipaso zokwatisa nazoso ziliko ngati mwazikonda
0990135851

Address

S112, Loudon
Mzuzu
35

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Adake Phule Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category