Bonkez chavula

Bonkez chavula WELCOME TO MY FACEBOOK PAGE🙏💪
💙BONKEY BONKEZ CHAVULA💙✅❇️
(5)

Mwamuna wanzeru amadziwa chosowa cha mkaz wake😁ndipo samadikira k*ti apemphedwe kaye ayi😋akaz ena kupempha ndikowavuta k...
25/06/2026

Mwamuna wanzeru amadziwa chosowa cha mkaz wake😁ndipo samadikira k*ti apemphedwe kaye ayi😋akaz ena kupempha ndikowavuta kwambr ❤️🤗

Good morning?🌄🌞

Girls mukazaona mamuna wangoyamba kukukondani mozipereka zaziweni k*ti ndarama zamuthera ndipo alibeso kopita kwina,kodi...
24/06/2026

Girls mukazaona mamuna wangoyamba kukukondani mozipereka zaziweni k*ti ndarama zamuthera ndipo alibeso kopita kwina,koditu vamuna ndivindeletu 🤣🙄🙄

Mamuna wapabanja sakhala ndimzake wamkazi chimodzi modziso mkazi wapabanja sakhalaso ndi zake wamamuma umenewo ndi uhule...
23/06/2026

Mamuna wapabanja sakhala ndimzake wamkazi chimodzi modziso mkazi wapabanja sakhalaso ndi zake wamamuma umenewo ndi uhule 😅

kaya zikumvekaa? 😂🙏

Ukafuna mkazi osakonda ndalama uwumbe wako,chifukwa mkazi amafunika ndalama k*t azioneka bwino kaya tikumvana azibambo👏🏿...
23/06/2026

Ukafuna mkazi osakonda ndalama uwumbe wako,chifukwa mkazi amafunika ndalama k*t azioneka bwino kaya tikumvana azibambo👏🏿😄

good morning family 🌞 🌅

Mzimu wanga ukundiuza k*ti my future wife akufuna data  😁Bea Ndilankhuleni Akhale a network yanji TNM kapena Airtel 🤣😂
22/06/2026

Mzimu wanga ukundiuza k*ti my future wife akufuna data 😁Bea Ndilankhuleni Akhale a network yanji TNM kapena Airtel 🤣😂

22/06/2026

Vuto la akadzi ama hipiwa amaganiza ngati amuna tonse timawafuna, enafe timakonda mapolo amagesi omwewa😂😂😂

19/06/2026

ndikudutsa munyengo zowawa muzindipemphelerako 🙏🙌😪😪

14/06/2026

amuna olongosokafe sitikakamira mkazi Kungotikana kamodzi basi kamaveka😂😂😂

mwaswera bwanji! 😅😅

13/06/2026

Kuli amuna andalama kunja kuno,koma sungave k*ti akwatira akaz awiri, koma winawe kungoweta abakha 4, mpaka mulu wa akaz🤣

Address

Brown Street Upington
Upington Outlying
801

Telephone

+265991529051

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bonkez chavula posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Upington Outlying?

Share