Mtumbati

Mtumbati Funny Village vs Town Experiences

Angakhale anyamata a boma lanji awa???
22/08/2026

Angakhale anyamata a boma lanji awa???

From inboxAti mukuganiza kuti ndi chifukwa chomveka kuti banja lithe??Nanga mutakhala inu bambo mungatipo chiyani?
21/08/2026

From inbox

Ati mukuganiza kuti ndi chifukwa chomveka kuti banja lithe??

Nanga mutakhala inu bambo mungatipo chiyani?

19/08/2026

Ngati mukusakasaka Heartbreak tsekulani ku inbox kwa wokondedwa wanuyo!

Mayi Lennie Mwase amangidwa atapezeka ndi mankhwala osiyanasiyana koma opanda zikalata zovomerezeka ku Mwanza.Katundu wa...
17/08/2026

Mayi Lennie Mwase amangidwa atapezeka ndi mankhwala osiyanasiyana koma opanda zikalata zovomerezeka ku Mwanza.

Katundu wa boma tiyeni tisamaleni

Momwe akuyankhira chemwalira inu mungaganize bwanji pamenepo??
17/08/2026

Momwe akuyankhira chemwalira inu mungaganize bwanji pamenepo??

17/08/2026

Koma imfa za ana achicheperezi mmm zimapweteka kwambiri...yes of course imfa ndi imfa.

17/08/2026

Ku Ntchisi mfumu yaikulu Kalumo aletsa zomangotengana ngati banja mosavomerezeka( Chikumu).

Akuti izi zikukolezera mchitidwe wokwatiritsa ana mu njira ya chikumu yomwe ndi yodziwika kwambiri madera ndi maboma ambiri mchigawo cha pakati.

Ndipo achenjeza kuti aliyense aphwanye lamuloli kuphatikizirapo mafumu omwe avomereze izi kuchitika mdera lake adzalandira chilango.

Kodi kwanuko mamuna ndi mkazi akakwatirana opanda dongosolo la chikhalidwe, chipembedzo kapena mthyathu mumautcha kuti chiyani??

17/08/2026

Woyimba uti atimenyere freestyle pano pa Mtumbati TV??

Tiuzeni mu comment section

16/08/2026

From inbox

Akuti potengera ndi zomwe wakumana nazo kwa achibale ake omwe anawayendera, akuti waganiza zosintha mkuluwiko woti " Ukayendera mzengo usamati asakhwi afumbula", kuti ukhale woti " Ukayendera achibale usamati udani palibe". Iye watero.

Address

Mwanza

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtumbati posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Mtumbati:

Shortcuts

Share

Category